Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Papa Francisco Wati Akhristu Akuyenera Kuyenda Mu Njira Ya Chiyembekezo.

$
0
0

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika-yu amalankhula izi ku likulu la mpingowu ku VATICAN pa mkumano omwe amakhala nawo lachitatu lililonse ndi anthu omwe amafika ndi kudzacheza ku likulu la mpingowu.

Iye wati wati akhristu akuyenera kutengera chitsanzo cha Abram yemwe anakhala Abraham kaamba koti anali ndi chiyembekezo pamene mulungu anamulonjeza kuti amupatsa mwana wamwamuna ngakhale anali wachikulire.

Pamenepa wati kudzera mwa Abraham akhristu akuyenera kutengerapo chitsanzo komanso akuyenera kuzindikira kuti pa kukhala mu chiyembekezo sakuyenera kuchita mantha kukumana ndi zovuta koma akuyenera kuzigonjetsa. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>