Afa Atagwera mu Mtsinje ndi Njinga
Mnyamata wina wa zaka khumi ndi zinayi (14) wafa atagwera mu mtsinje wina m’boma la Mangochi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Inspector Rodrick Maida, wati m’mawa wa lero pa 4 January 2018,...
View ArticleObama Awonjezera Ndalama Za Chikho
Nduna ya zophunzitsa anthu, chikhalidwe ndi chitukuko cha ku midzi, mayiGrace Chiumiayawonjezera ndalama za mu ligi ya mpira wa miyendo yomwe imadziwika ndi kuti Obama Football League, yomwe...
View ArticleRed Cross Ipempha Mabungwe Agwilire Ntchito Limodzi
Bungwe laMalawi Red Cross Societylapempha mabungwe omwe siaboma kuti azilumikizana pomwe akugwira ntchito zosiyanasiyana zokhudza ngozi zogwa mwadzidzi. Mkulu wa bungweli m’boma la Zomba, aBlessings...
View ArticleMphunzitsi Azipha Pozimangilira M’boma la Dedza
Bambo wina wa zaka 47zakubadwawadzipha podzimangilira m’boma la Dedza. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Edward Kabango, bambo-yu ndi Ives Kumankhamba ndipo anali mphunzitsi pa sukulu...
View ArticleDziko La Zimbabwe Likufufuza Momwe Grace Mugabe Anapezera PhD Yake
Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu mdziko laZimbabwelikuchita kafukufuku wofuna kupeza ngati mkazi wa mtsogoleri wakale wa dzikolo aGrace Mugabeanapeza certificate yake yaPhDmwachinyengo....
View ArticleKuphwera kwa Nyanja ya Chilwa Kwadzetsa Njala
Anthu okhala mdera lozungulira nyanja ya Chirwa m’boma la Zomba ati ali pa mavuto a njala ya dzawoneneni kutsatira kuphwera kwa nyanja ya Chilwa. Mfumu Njala ya kwa Sub T/A Nkagula m’bomalo yauza Radio...
View ArticleMkwamba Akhala Nambala 2 Polemba Nkhani Za Masewero
Wolemba nkhani zamasewero ku Radio Maria Malawi Foster Mkwamba wakhala m’modzi mwa atolankhani omwe achita bwino polemba nkhani za masewero mu mpikisano wa FIFA/FAM Under 20, mchaka cha 2017. Mkwamba...
View ArticleNRB Ikupitiriza Kulemba Anthu Mkaundula wa Unzika
Bungwe lowona za kalembera mdziko muno la National Registration Bureau (NRB) lalengeza kuyambiranso kwa ntchito yolemba anthu mu kaundula wauzika mdziko muno. Wofalitsa nkhani ku bungweli a Norman...
View ArticleEthiopia Yaletsa Kupereka Ana Mmaiko Ena
Dziko la Ethiopia laletsa mchitidwe opereka ana kwa mzika za m’maiko ena, zomwe zimafika mdzikolo kufuna ana oti adzikawasamalira. Ganizoli, ladza, boma litalandira malipoti oti ana otengedwa ndi...
View ArticleKuchuluka Kwa Zipani Kulibe Vuto, Koma...
Mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Umodzi, Professor John Chisi wati sakuwonapo vuto pa kuchulukana kwa zipani za ndale mdziko muno. Professor Chisi wanena izi polankhula ndi Radio Maria Malawi....
View ArticleNICE Ilonjeza Kulumikiza Adindo ndi Anthu Awo Mboma La Balaka
Bungwe lophunzitsa anthu pa zinthu zosiyanasiyana la Nice-Trust m’boma la Balaka, latsimikizira anthu m’bomalo kuti liwonetsetsa kuti labweretsa pamodzi makomiti a chitukuko ndi adindo awo ndi cholinga...
View ArticleBoma Liyamikira SRWB
Boma layamikira bungwe la Southern Region Water Board kaamba kokwanitsa kupereka madzi aukhondo kwa makasitomala ake. Nduna ya zamalimidwe, ulimi wa nthilira ndi chitukuko cha madzi a Joseph...
View ArticleAnthu Anayi Afa Kaamba ka Mphepo ya Mkuntho ku Ulaya
Anthu anayi afa kaamba ka mphepo ya mkuntho yomwe ikuwomba m’maiko a kumpoto kwa chigawo cha ulaya. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu atatu afa mdziko la Netherlands ndipo m’modzi wafa mdziko la...
View ArticleBambo Tonny Mukomba Ayikidwa M’manda Loweruka
Mwambo woyika m’manda thupi la malemu bambo Tony Mukomba omwe amatumikira mu arkidayosizi ya mpingo wa katolika ya Blantyre, udzachitika loweruka likudzali pa 20 January 2018. Malinga ndi a kuofesi...
View ArticlePapa Auza Achinyamata Akhale Olumikizana Ndi Yesu Khristu
Msogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco walimbikitsa achinyamata a mdziko la Chilekuti akhale olumikizana bwino ndi Yesu Khristu monga momwe amalumikizirana kupyolera pa zida za...
View ArticleMadeira Apempha Manoma Adekhe
Timu ya Mighty Beforward Wanderers yati zokonzekera zake zotenga nawo mbali mu mpikisano wa CAF Champions League zikuyenda bwino. Polankhula ndi Radio Maria Malawi, m’modzi mwa akuluakulu ku timuyi...
View ArticleBambo Mukomba Alowa M’manda
Mwambo woyika m’manda thupi la malemu bambo Tony Mukomba omwe amatumikira mu arkidayosizi ya Blantyreya mpingo wakatolika, wachitika lero ku Limbe Cathedral mu Ark dayosiziyo. Arkepiskopi wa...
View ArticleAnthu 15 Afa ndi Kuzizira kwa Snow Mdziko la Lebanon
Anthu othawa kwao khumi ndi asanu a mdziko la Syria apezeka atafa ndi kuzizira kwa snow pomwe amafuna kuwoloka mapiri a mdziko la Lebanon omwe anachita malire ndi dziko la Syria. Malipoti a wailesi ya...
View ArticleBambo Abisalom Ayikidwa Lolemba
Akulikulu la mpingo wakatolika m’dziko muno alengeza za imfa ya bambo Juliano Absalom, omwe amatumikira mu dayosizi ya Dedza. Malingana ndi chikalata chomwe a ku likululi atulutsa, bambo Absalom...
View ArticlePapa Wapempha Anthu Mdziko la Peru Kuti Alimbane ndi Katangale, Kuwonongeka...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, walimbikitsa anthu ogwira ntchito zosiyanasiyana mdziko la Peru, kuti adzigwira ntchito zawo ndi chikhulupiliro, makanso pamene akulimbana...
View ArticleMabungwe Omwe Si Aboma Atenge Mbali Polimbana Ndi Kolera
Mabungwe omwe si aboma m’boma la Zomba awapempha kuti agwire ntchito limodzi ndi unduna wa zaumoyo pophunzitsa anthu ntchito yolimbana ndi matenda a kolera m’bomalo. Mkulu wa za umoyo m’boma la Zomba a...
View ArticleKuchepa Kwa Chindapusa Kukuwonongetsa Chilengedwe
Kuchepa kwa chindapusa chomwe bwalo la milandu limapereka kwa anthu omwe apezeka akudula mitengo m’malo oletsedwa ati kukubwezeretsa m’mbuyo ntchito yobwezeretsa chilengedwe mdziko muno. Wachiwiri kwa...
View ArticleZaka 15 Kaamba Koba Mowopseza Ndi Mfuti
Bwalo lamilandu m’boma la Mangochi dzulo lalamula amuna atatu kuti akakhale kundende kwa zaka khumi ndi zisanu 15 aliyense, atapezeka olakwa pa mlandu wakuba mowopseza ndi mfuti. Wachiwiri kwa mneneri...
View ArticleAnthu 37 Afa pa Ngozi ya Moto Mdziko la South Korea
Anthu pafupifupi 37 afa ndipo ena oposera 70 avulala kaamba ka moto omwe unabuka pa chipatala china cha Sejong mdziko la South Korea. Pa nthawi yomwe motowu umayamba kubuka, mu chipatalachi munali...
View ArticlePapa Afunira Zabwino Nthumwi za Bungwe la World Economic Forum
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wafunira zabwino nthumwi zomwe zikuchita nawo msonkhano wa bungwe loona za kayendetsedwe kabwino ka chuma la World Economic Forum umene...
View ArticleAnthu 100 Afa Mdziko la Afghanstan
Anthu oposera 1 hundred afa mu mzinda wa Kabul mdziko la Afghanstan kaamba ka mabomba omwe anaphulitsidwa mu mzindawu. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu omwe achita chiwembuchi anayika mabombawa mu...
View ArticleBambo Robert Masinda a Mdziko la DRC Apezeka Alibwino
Mpingo wakatolika m’dziko la Democratic Republic of Congo(DRC) wati ndi wokondwa ndi kumasulidwa kwa bambo Robert Masinda, ndi anthu ena asanu, omwe anagwidwa ndi gulu lina la zigawenga m’dzikomo....
View ArticlePapa ndi Okhudzidwa ndi Imfa ya Anthu 37 Mdziko la South Korea
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse, Papa Francisco wati ndi wokhudzidwa ndi imfa ya anthu omwe afa pangozi ya moto umene unabuka pa chipatala cha Sejong m’dziko la South Korea. Papa, wati...
View ArticlePMS Iyamikira a Khristu Pothandiza pa Chaka cha Epifania
Ofesi yoona za mabungwe a utumuki wa a papa ku likulu la mpingo wakatolika m’dziko muno ya Ponfitical Mission Societies(PMS) yayamikira chidwi chomwe akhristu a mpingowu anaonetsa pothandiza kuti...
View ArticleMpingo wa CCAP Upemphelera Mvula
Mpingo wa CCAP mu Sinodi ya Blantyre wachita mapemphero apadera, opempha mulungu, kuti adalitse dziko lino ndikulipatsa mvula yabwino. M’modzi mwa akulu-akulu mu mpingo-wu, m’busa Alex Maulana, wati...
View ArticleAnthu 400 a Malawi Young Pioneer Alandirapo Zawo
Unduna wa zachuma mdziko muno ati walipira ndalama kwa anthu oposa400 omwe anali a Malawi Young Pioneer omwe anakhudzidwa ndi Operation Bwenzani. Mneneri mu undunawu a Davis Sado auza Radio Maria...
View ArticlePapa Ayamikira Bungwe la Redcross Mdziko la Italy
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wauza bungwe lomwe limapereka thandizo kwa anthu omwe akumana ndi mavuto a njala,nkhondo, matenda ndi zina la Italian Red Cross kuti...
View ArticleMilandu Itatu Yogwilira ku Chikwawa Mwezi wa January
Apolisi m’boma la Chikwawa akusunga m’chitokosi bambo wina wa zaka 20za kubadwa yemwe dzina lake ndi William Masiyamphuka, kaamba komuganizira kuti wagwilira m’sungwana wa zaka zisanu. Padakalipano...
View ArticleMakwaya Ayike Chikhristu Patsogolo
Makwaya a mu mpingo wakatolika ati akuyenera kuzindikira kuti akuyenera kuyika chikhristu patsogolo pogwira ntchito zawo mu mpingo. Bambo Lawrence Kudzingo otumikira mu dayosizi ya Dedza ndi omwe...
View ArticleSister Apempha Papa Akambirane ndi Zigawenga za Al-Quaeda
Sisiteri wa m’dziko la Colombia yemwe akusungidwa mokakamiza ndi zigawenga za Al-Qaeda mdziko la Mali, wapempha mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco kuti athandize pa ntchito...
View ArticleECM Ilankhula pa za Nsalu Yodabwitsa pa Msika
Mpingo wa katolika mdziko muno wapempha akhristu ake kuti asagule nsalu yomwe ikupezeka pa msika yomwe ikusonyeza mayina a Papa Franciscko, Benedict 16. Mlembi wamkulu wa bungwe la ma episkopi a mpingo...
View ArticleApezeka Atafa Podzimangilira
Bambo wina wa zaka 37 zakubabdwa wapezeka atafa pozimangilira kwa Chikanda mu mzinda wa Zomba. Mneneri wa apolisi m’chigawo cha kummawa kwa dziko lino Inspector Joseph Sauka wauza Radio Maria Malawi...
View ArticleKabwerebwere Alamulidwa Zaka 9 ku Ndende
Bambo wina wa zaka 32 zakubadwa amulamula kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavulagaga kwa zaka zisanu kaamba kothyola shop ndi kuba katundu wa ndalama za nkhaninkhani. Wachiwiri kwa...
View ArticleKhoti Lidzamvanso Mlandu wa a Chaponda pa 8 February
Bwalo la Chief Resident Magistrate m’boma la Zomba, likuyembekezeka pa 8 mwezi uno kuzapitirira kumva mlandu wa nduna ya kale ya zamalimidwe a George Chaponda omwe akuwazenga mlandu powaganizira kuti...
View ArticleMabungwe, MACRA Amemeza Anthu Akalembetse ma Sim Card
Mabungwe omwe si aboma ati akugwilizana ndi njira yoti aliyense akalembetse simu-kadi yake ya foni kamba koti zimenezi ndi zothandiza pa chitetedzo cha onse omwe amagwilira ntchito njirayi polumikizana...
View ArticleAfa Atawombedwa ndi Galimoto ku Ntchisi
Bambo wina wafa ataombedwa ndi njinga ya moto m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Sergeant Gladson Mbumpha wati a Bruno Malithano a zaka 38zakubadwa anakwezana njingayo yomwe ndi...
View ArticleAtolankhani Atenge Mbali Poteteza Anthu Achikulire
Bungwe lomenyera ma ufulu a anthu achikulire, la Malawi Network of Older People (MANEPO) lati atolankhani ndi ofunika pa ntchito yoteteza maufulu a anthu achikulire mdziko muno. Mkulu wa bungweri a...
View ArticleBwanamkubwa wa Balaka Apempha Mgwirizano
Khonsolo ya boma la Balaka yapempha kuti pakhale ubale wabwino pakati pa adindo ndi makomiti a za chitukuko m’bomalo. Bwanamkubwa wa bomalo, Rodrick Mateauma ndi yemwe wanena izi potsatira mphekesera...
View ArticleChipani cha MCP Sichikudziwapo Kanthu pa “Antchito”
Chipani cha Malawi Congress(MCP) chati sichikudziwapo kanthu kwa achinyamata omwe akuti anabwera ku likulu la chipanichi m’chigawo cha ku m’mwera kudzafuna malipiro awo a ntchito. Wapampando wa chipani...
View ArticleMACRA Ikondwelera Tsiku Lokumbukira Wailesi pa Dziko Lonse
Dziko laMalawimawa ligwilizana ndi mayiko pa dziko lonse pochita mwambo wa tsiku loganizira nyumba zoulutsira mawu padziko lonse (World Radio Day). Mwambo wa ukulu woganizira tsikuli unachitikira ku...
View ArticleGogo Afa Khoma la Nyumba Litamugwera
Mayi wina wafa khoma la nyumba litamugwera m’boma laNtchisi. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomaloSergeantGladson Mbumpha,malemu mayiMelina Felix akuti khudzidwa ndi imfayi pa nthawi imene...
View ArticleTsvangirai Wamwalira
Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma ku nyumba ya malamulo mdziko la Zimbabwe, Morgan Tsvangirai wamwalira. Malipoti a wailesi ya BBC ati Tsvangirai wamwalira pa chipatala china cha mdziko la South...
View ArticleSam Mpasu Wamwalira
Mtsogoleri wa chipani cha New Labour, a Sam Mpasu apezeka atafa ku nyumba kwawo. Mneneri wa ku banja a Stanly Wasi, ati akukhulupilira kuti a Mpasu omwe anakhalaponso sipikala wa nyumba ya malamulo...
View ArticleZuma Atula Pansi Udindo
Mtsogoleri wa dziko la South Africa, Jacob Zuma watula pansi udindo wake. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, Zuma wati akuchoka pa udindowu mwa kufuna kwake osati kaamba kokakamizidwa ndi chipani...
View ArticleApha Msuweni Kaamba Kogona ndi Mkazi Wake
Apolisi m’boma la Mchinji amanga mamuna wina kaamba komuganizira kuti anapha msuweni wake atamugwira akuchita zadama ndi mkazi wake. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Inpector Kaitano...
View Article