Amuna Awiri Afa Pofukula Chitsime
Amuna awiri afa pomwe amafuna kufukula chitsime chakuphwa m’mudzi mwa Kadula m’dera la mfumu yayikulu Mlonyeni m’boma la Mchinji. M’neneri wa apolisi m’bomalo Detective Passwell Manase Phiri wati anthu...
View ArticleAnthu Mdziko Muno Adzipereke pa Ntchito za Chitukuko
Bungwe la Eye For Development lapempha amalawikuti azidzipereka pa ntchito zosiyanasiyana za chitukuko zomwe boma limakhala nazo pofuna kupititsa patsogolo miyoyo ya anthu mdziko muno. Mkulu wa...
View ArticleMamuna Wina M’boma la Ntchisi Amugamula kuti Akakhale ku Ndende Pafupifupi...
Bwalo loyamba lamilandu m’boma la Ntchisi lalamula mamuna wina wa zaka 27 zakubadwa kuti akakhale kundende kwa miyezi makumi atatu, atapezeka olakwa pa mlandu opanga kalata za chinyengo ndi cholinga...
View ArticleNthambi ya Zamaphunziro Ilimbikitsa Maphunziro mu Dayosizi ya Mangochi
Nthambi yowona za maphunziro ya mpingo wakatolika mu dayosizi ya Mangochi yati ichita chotheka kulimbikitsa maphunziro mu dayosiziyi mmasukulu amene ali achikatolika. Mmodzi mwa akuluakulu ku bungweli...
View ArticleAkhristu Akhale Patsogolo Kuthandiza Anthu Okhudzidwa ndi Madzi Osefukira
Parish ya St Pius mu Archdayosizi ya Blantyre, yalangiza maparish onse a mpingowu m’dziko muno, kuti akhale patsogolo pothandiza anthu omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira. Wapampando wa parishiyi a...
View ArticleAbwenzi A Radio Maria Agula Zipangizo Zokhazikitsira Transmitter
Abwenzi a Radio Maria Malawi mu Archdayosizi ya Blantyre awayamikira pa ntchito yopambana yomwe agwira pogula zipangizo za pa transmitter za ndalama zokwana 5.9 miliyoni kwacha. Polankhula pa mwambo...
View ArticleDziko la Nigeria Lalephera Kuteteza Mzika Zake
Bungwe lowona za ufulu wa anthu padziko lonse la Amnesty International,lati dziko la Nigeria lalephera kuteteza mzika zake zomwe zikukhala mdera la Baga,pamene gulu la zigawenga la Boko Haram lawopseza...
View ArticleMabungwe Achitepo Kanthu kwa Anthu Okhudzidwa ndi Kusefukira kwa Madzi
Bungwe lowona ma ufulu a anthu mchipembedzo cha Chisilamu la Muslim Forum for Democracy lalangiza mabungwe omenyera ufulu wa anthu mdziko muno,kuti athandize anthu omwe akhudzidwa ndi mvula ya mphamvu...
View ArticleAbambo Ali ndi Udindo pa Ana Awo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati abambo ali ndi udindo wawukulu pa miyoyo ya ana awo m’banja. Papa, amalankhula izi dzulo pa mwambo wa mapemphero womwe amakhala nawo...
View ArticleBungwe la ECM Lapempha Anthu Kuti Athandize Anthu Omwe Akhudzidwa ndi...
Bungwe la ma Episkopi la Episcopal Conference of Malawi (ECM), lapempha akatolika komanso anthu ena akufuna kwabwino kuti athandize anthu omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira mmaboma ambiri mdziko...
View ArticleDziko la Egypt Lalimbikitsa Ufulu wa ChipembedzoDziko la Egypt Lalimbikitsa...
Mpingo wa katolika mdziko la Egypt, wayamikira utsogoleri watsopano omwe uli mdzikolo kamba kolimbikitsa ufulu wa zipembedzo. Ofalitsa nkhani za mpingowu mdzikolo Bambo Rafic Greiche apereka chitsanzo...
View ArticleBungwe La Cadecom Aliyamikira Chifukwa Chopereka Thandizo
Khonsolo ya boma la Machinga, yayamikira bungwe lowona za chitukuko mu mpingo wakatolika la Cadecom mu Dayosizi ya Zomba, kamba ka thandizo lomwe bungweli likupereka kwa anthu omwe akhudzidwa ndi mvula...
View ArticleDziko la Egypt Lirimbikitsa Ufulu wa Chipembedzo
Mpingo wa katolika mdziko la Egypt, wayamikira utsogoleri watsopano omwe uli mdzikolo kamba kolimbikitsa ufulu wa zipembedzo. Ofalitsa nkhani za mpingowu mdzikolo Bambo Rafic Greiche apereka chitsanzo...
View ArticleBungwe la Cadecom Aliyamikila Chifukwa Chopereka Thandizo
Khonsolo ya boma la Machinga,yayamikira bungwe lowona za chitukuko mu mpingo wakatolika la Cadecom mu Dayosizi ya Zomba, kamba ka thandizo lomwe bungweli likupereka kwa anthu omwe akhudzidwa ndi mvula...
View ArticleLikulu la Mpingo Wakatolika Lapempha Bungwe la UN kuti Liteteze Amayi
Likulu la mpingo wa katolika pa dziko lonse ku Vatican,lapempha bungwe la mgwirizano wa mayiko la United Nations,kuti lichitepo kanthu pofuna kuteteza amayi maka achikhristu mmayiko momwe muli nkhondo...
View ArticleAnthu Osadziwika Athyola Tchalitchi Lina la Katolika Mdziko la India
Anthu omwe sakudziwika athyola tchalitchi la mpingo wakatolika mu mzinda wa New Delhi mdziko la India. Anthuwo akuti athyola chipata chachikulu cholowera mtchalitchilo ndipo atalowa mkati, aphwanya...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Idayamba Kale Kutolera Thandizo
Dayosizi ya Mangochi yati idayamba kale kukonzekera ntchito yotolera thandizo lothandizira anthu okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi. Polankhula ndi mtolankhani wathu, mlembi wa Episkopi wa dayosiziyi...
View ArticleDayosizi ya Zomba Ikufufuza Njira Zofuna Kupeza Thandizo Lokwanira...
Pofuna kupeza thandizo lokwanira lopita kwa anthu omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira potsatira pempho la maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko muno,dayosizi ya Zomba ya mpingowu, yati ikufufuza njira...
View ArticleAtsogoleri Achisilamu Adzudzula Gulu la Zigawenga za Islamic State
Atsogoleri a chisilamu m’mayiko osiyanasiyana, adzudzula gulu la zigawenga za Islamic State I.S, lomwe posachedwapa linatulutsa kanema yemwe akuwonetsa mamembala a gululi, akupha munthu wina oyendetsa...
View ArticleAtolankhani Azilemba Nkhani za Matenda Osapatsirana
Atolankhani mdziko muno awapempha kuti azilemba nkhani zokwanira zokhudza matenda osapatsirana omwe ndi kuphatizapo a shuga pofuna kuchepetsa imfa zomwe zimachitika kudzera mmatendawa. Mkulu wa bungwe...
View Article