Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Chipani cha Democrat Mdziko la America Chikufuna Mavoti Awerengedwenso

$
0
0

Anthu otsatira chipani cha Democrat mdziko la America ati akufuna kuti mavoti a chisankho chomwe chachitika  posachedwapa mdzikolo awerengedwenso.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC anthuwa anena izi poganiza kuti makina a computer omwe amagwiritsa ntchito panthawiyi anali ataonongeka.

Iwo ati pa nthawi yokopa anthu yemwe amaimira chipinichi a Hillary Clinton anali ndi anthu ambiri owatsatira kusiyana ndi a Donald Trump omwe anapambana pachisankhochi zomwe ati a Clinton anayenera kupambana.

ADonald Trump anapambana pachisankhochi ndi ma voti pafupifupi 280 ndipo akuyembekezeka kukalowa ku nyumba ya boma ya dzikolo pa 20 January chaka cha mawa. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>