Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Njala Ikubwezeretsa Ntchito Za Chitukuko

Mavuto anjala ati akubwezeretsa m’mbuyo ntchito za chitukuko komanso maphunziro ku dera la kum’mwera kwa boma la Neno. Phungu wa derali Mayi Mary Maulidi ndi omwe anena izi pomwe bungwe lina lomwe sila...

View Article


Bungwe la Amayi Lilonjeza Kutukula Dayosizi

Wapampando watsopano wa bungwe la amayi mu mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba , Mayi Elizabeth Meke wati komiti yawo ipitiliza kudzipeleka pa ntchito zotukula dayosiziyo. Mayi Mekeanena izi...

View Article


Mpingo wa Anglican Ukulimbikitsa Maphunziro a Atsikana

Mpingo wa Anglican mu dayosizi ya Uppershire kudzera mu project yomwe mpingowu unakhadzikitsa ya Msamama Community Intergrated wati upitiliza kudzipeleka polimbikitsa maphunziro atsikana. Mkulu...

View Article

Anthu 142 Avulala pa Ngozi ya Sitima Mdziko la India

Anthu 142 ati afa ndipo ena oposa 200 avulala stima ya pa mtunda yomwe anakwera itachita ngozi mu mzinda wa Pradesh kumpoto kwa dziko la India. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBCanthu pafupifupi 58...

View Article

Papa Wati Chitseko Cha Chifundo Chidakali Chotsekula

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati akhristu akuyenera kuzindikira kuti chitseko cha chifundo chimakhala chotsekula nthawi zonse ngakhale chitseko choyera chatsekedwa...

View Article


Alamulidwa Kukakhala ku Ndende Zaka Zitatu Kamba Kogona Ndi Mnyamata Wopempempha

Bwalo loyamba la milandu m’boma la Machinga lalamula mzimayi wina wa zaka 26 zakubadwa kuti akakhale kundende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka zitatu kaamba kopezeka olakwa pa mlandu...

View Article

Chipani cha Democrat Mdziko la America Chikufuna Mavoti Awerengedwenso

Anthu otsatira chipani cha Democrat mdziko la America ati akufuna kuti mavoti a chisankho chomwe chachitika  posachedwapa mdzikolo awerengedwenso. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC anthuwa anena...

View Article

Papa Achita Mkumano ndi Akulu Akulu a Zipembedzo Mdziko la Iraq

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ati anachita mkumano ndi akuluakulu owona za chikhalidwe cha chipembedzo cha chisilamu komanso owona za ubale a mipingo ya chikhristu a...

View Article


Parish Ya CI Ikufuna 5 Million Kwacha Kuti Itsilizire Tchalitchi

Parishi ya mpingo wakatolika ya St. Louis Montfort CI   mu arkdayosizi ya Blantyre yapempha anthu akufuna kwabwino kuti achitepo kanthu pomaliza kumanga tchalitchi lawo. Mmodzi mwa akuluakulu a...

View Article


Apolisi M’boma la Mangochi Akusaka Zigawenga Zisanu

Apolisi m’boma la Mangochi ati akufunafuna anthu ena asanu omwe sakudziwika omwe anapita kukaba ndi zikwanje kwa mzika ina ya mdziko la India. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergent...

View Article

Matupi 32 Komanso Mitu 9 Zapezeka Zitakwiliridwa Mdziko la Mexico

Akuluakulu a mdziko la Mexico ati apeza matupi a anthu makumi atatu ndi awiri 32 komanso mitu ya anthu isanu ndi inayi 9 itakwililidwa mdera lina lomwe zigawenga zomwe zimagwiritsa ntchito mankhwala...

View Article

Alamulidwa Kukakhala ku Ndende kwa Zaka 15 pa Mlandu Wozembetsa Ana

Bwalo la milandu m’boma la Zomba lalamula mamuna wina wa zaka 28 zakubadwa kuti akhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka khumi ndi zisanu kaamba kopezeka olakwa pa mlandu wa...

View Article

Kusowa Masomphenya Kukuchititsa a Ndale Kusakhazikika M’chipani Chimodzi

Kusowa kwa masomphenya a zipani zandale zosiyanasiyana mdziko muno akuti ndi komwe kukuchititsa atsogoleri azipani zina  kusakhazikika mu chipani chimodzi. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha...

View Article


ECM Ipempha Akhristu Atenge Mbali Pa Ulendo Wa Ndawala

Mpingo wa katolika mdziko muno molumikizana ndi mpingo wa evangelical wapempha akhristu onse mdziko muno kuti atenge nawo mbali pa ulendo wa ndawala womwe wakonzedwa kuti uchitike pa 6 mwezi wa mawa....

View Article

Wakuba wa pa Facebook Wagwidwa

Apolisi ku Namadzi m’boma la Chiradzulu agwira m’nyamata wina yemwe wakhala akubera anthu kudzera pa makina a internet makamaka facebook ndi njira zina. Mkulu wa polisi ya Namadzi, Assistant...

View Article


Apolisi Agwira Anthu Opezeka ndi Mankwala, Chamba

Apolisi m’boma la Mangochi amanga bambo wina wa zaka 65 zakubadwa kaamba kopezeka ndi mankhwala popanda chilolezo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo sergeant Amina Tepani Daudi wati dzulo, apolisi...

View Article

Anthu Awiri Afa pa Ziwawa Mdziko la Zambia

Anthu awiri afa, anthu ena atawaotcha ndi moto potsatira ziwawa zomwe anthu m`dziko la Zambia  akuchitira  anthu obwera (Xenophobia) mu mzinda wa Lusaka. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, anthu...

View Article


Unduna Upempha Anthu Asamukire Kumadera Okwera

Unduna woona za ulimi wa mthirira ndi chitukuko cha madzi wapempha anthu omwe akukhala m`madera otsika m`boma la Karonga kuti asamukire kumadera okwera.   Unduna wu wanena izi kudzera m`chikalata...

View Article

Galimoto za Diesel Zitha Pofika 2025

Akuluakulu a mizinda inayi ikuluikulu komanso yotchuka pa dziko lonse ati akufuna kuthetsa magalimoto oyendera mafuta a diesel pofika m’chaka cha 2025. Malipoti a wailesi ya BBC ati ma mayor a mizinda...

View Article

Apempha a Malawi Asakopeke ndi Anthu a Kunja

Nthambi yoona zolowa ndi kutuluka ya Immigration pa chipata cha Chiponde m’boma la Mangochi yapempha anthu m’dziko muno kuti apewe kukopeka ndi anthu omwe akumabwera m’madera osiyanasiyana ndi kumawuza...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>