Mwambo woyika m’manda imodzi mwa mafumu odziwika pa nkhani yolimbikitsa zitukuko m’dziko muno Themba Nthalire ya m’boma la Chitipa uchitika pa 12th August 2017 kulikulu la mafumu m’boma la Chitipa.
Mfumu-yi inamwalira la chitatu pa 12th August 2017 ku chipatala cha Ekwendeni m’boma la Mzimba .
Mfumuyi inabadwa pa pa 12th May mchaka cha 1926 ndipo ndi imodzi mwa mafumu amene akhala pa ntchito zotukula dera lawo ndi dziko lino.