Likulu la Mpingo Wakatolika pa Dziko Lonse Liyamikira Dziko la Malawi
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awayamikira kamba kopeleka molowa manja m’miyambo yonse yomwe mpingowu umakhala ukupempha thandizo kuchokera kwa iwo. Likulu la mpingowu ku Rome m’dziko la...
View ArticleAnthu Alimbike Pothetsa Mchitidwe Wozembetsa Anthu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati anthu akuyenera kugwira ntchito molimbika pofuna kuthetsa mchitidwe wozembetsa anthu. Papa amalankhula izi lamulungu pa ku likulu la...
View ArticleZigawenga za IS Zichita Chiwembu ku Ofesi ya Kazembe wa Dziko la Iraq
Kumenyana kwa mphamvu kwabuka pakati pa asilikali a mdziko la Afghanistan ndi zigawenga za chisilamu za Islamic State potsatira chiwembu chomwe zigawengazi zinakachita ku ofesi ya kazembe wa dziko la...
View ArticleGalimoto Lapha M’modzi ndi Kuvulaza Atatu M’boma la Mangochi
Galimoto lina lomwe woyendetsa wake sakudziwika ati lapha m’nyamata wa zaka khumi ndi zinayi (14) ndi kuvulaza ena atatu m’boma la Mangochi. Malinga ndi wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi m’boma...
View ArticleBambo Wina Adzipha Ku Nkhotakota Pa Nkhani Za M’banja.
Bambo wina wa zaka 25 zakubadwa m’boma la Nkhotakota wadzipha podzimangilira atamvetsedwa kuti mkazi wake akuchita chibwenzi cha nseli ndi mwamuna wina. Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za...
View ArticleAnankungwi Ndi Angaliba Awapempha Kuti Atulutse Msanga Zinamwali.
Mfumu Mpinganjira ya m’dera la mfumu yayikulu Mponda m’boma la Mangochi yapempha omwe alowetsa zinamwali m’bomali kuti adzatulutse mwansana zinamwalizo. Iyo yati kutulutsa nsanga zinamwali...
View ArticleBomba Lapha Anthu Khumi Mdziko la Pakistan
Anthu khumi afa ndipo ena makumi atatu avulala potsatira bomba lomwe linaponyedwa pa bwalo lina lozengera milandu mu mzinda wa Mardan kumpoto kwa dziko la Pakistan. Malipoti a wailesi ya BBC ati munthu...
View ArticleAmayi awapempha kuti aziyamwitsa ana awo mkaka wa m’mawere moyenera.
Bungwe la za umoyo pa dziko lonse la World Health Organization (WHO) lati amayi akuyenera kumayamwitsa ana awo mkaka wa mmawere ndi cholinga choti anawo azikula ndi thanzi labwino. Polankhula...
View ArticleBomba Lapha Anthu Khumi Mdziko la Pakistan
Anthu khumi afa ndipo ena makumi atatu avulala potsatira bomba lomwe linaponyedwa pa bwalo lina lozengera milandu mu mzinda wa Mardan kumpoto kwa dziko la Pakistan. Malipoti a wailesi ya BBC ati munthu...
View ArticleZARDD Ikuchepetsa Njala ku Chingale Kudzera mu Ulimi Wamthilira
Anthu a m’dera la Chingale m’boma la Zomba ati ndi okhutira ndi ntchito zomwe nthambi ya chitukuko ya dayosizi ya Zomba ya Zomba Diocese Research and Development (ZARDD) ikugwira m’derali pothandiza...
View ArticleMabanja Awalimbikitsa Kulembetsa Maina Awo.
Akhristu a mu Arch-Dayosizi ya Blantyre awapempha kuti alembetse maina awo kuti azatenge nawo mbali pa sonkhano waukulu wa mabanja omwe uzachike kuyambira pa 4 ndi kutha pa 5 August mu Arch-Dayosizi ya...
View ArticleMaphunziro A M’mera Mpoyamba ndiofunika Kwa Ana.
Bungwe la Future Vision Ministry lapempha makolo a mdera la Sub T/A Ngwelero m’boma la Zomba kuti azikhala ndi chidwi chotumiza ana awo sukulu za m’mera mpoyamba. Mkulu wa bungweli a Newton Sindo ndi...
View ArticleMphunzitsi wamkulu Afa Pozimangilira.
Mphunzitsia wamkulu wa pa sukulu ya pulaimale m’boma la Dowa wazipha pozimangilira kudenga la nyumba yake. Malinga ndi ofalitsa za apolisi m’bomalo Sergent Richard Kaponda wati mphunzitsiyu ndi Briay...
View ArticleT/A Nthalire Ya KuChitipa Iyikidwa M’manda .
Mwambo woyika m’manda imodzi mwa mafumu odziwika pa nkhani yolimbikitsa zitukuko m’dziko muno Themba Nthalire ya m’boma la Chitipa uchitika pa 12th August 2017 kulikulu la mafumu m’boma la Chitipa....
View ArticleAmayi Awapempha Kuti Azithandiza Amayi Anzawo Ovutika.
Amayi a mpingo wakatolika awapempha kuti adzipereke pa ntchito yothandiza amayi anzawo omwe akukomana ndi mavuto osiyanasiyana m’dziko muno. Mkazi wa wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino , mayi Mary...
View ArticleAmsembe A Ku Chikwawa Azamitsa Moyo Wawo Wa Uzimu.
Amsembe a mpingo wakatolika mu dayosizi ya Chikwawa anakumana malo amodzi ndi kuzamitsa moyo wawo wa uzimu ku dzera mu mbindikiro wawo umene anali nawo kuyambira pa 6 august ndi kutha pa 11 mwezi uno....
View ArticleDziko la China Lamanga Episkopi Wodzalowa M’malo Mwa Bishop Wopuma
Akuluakulu a dziko la China ati amanga episkopi wodzalowa m’malo mwa bishop wopuma wa mpingo wakatolika ndi kumuchotsa ku dayosizi yomwe amatumikira pofuna kuti asakhazikitsidwe kukhala episkopi...
View ArticleApempha Amwenye Ndi Ma China Kuti Azithandiza Apolisi
Mkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mawa kwa dziko lino commisioner Marther Suwedi wapempha anthu ochita malonda mu m’dzinda wa Zomba kuti adzidzipeleka pothandiza apolisi pa ntchito zolimbikitsa za...
View ArticleRAC Ifalitsa Mauthenga Okhudza Human Trafficking M’boma La Mangochi
Anthu a m’dera la mfumu yayikulu Mponda m’boma la Mangochi awazindikilitsa za momwe anangapewere ndi kuzindikira anthu amene amalimbikitsa m’chitidwe wozembetsa ndi kugulitsa anthu Human Trafficking....
View ArticleNtchito Yokhadzikitsa Bungwe La Kolona Ikuyenda Ku Zomba.
Ntchito yokhadzikitsa bungwe lolimbikitsa mapemphero a kolona m’maparishi osiyanasiyana akuti ikuyenda bwino mu dayosizi ya zomba. Mkulu wa bungwe-li a Grasiano Mukunuwa ndi omwe anena izi polankhula...
View Article