Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Apempha Amwenye Ndi Ma China Kuti Azithandiza Apolisi

$
0
0

Mkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mawa kwa dziko lino commisioner Marther Suwedi wapempha anthu ochita malonda mu m’dzinda wa Zomba kuti adzidzipeleka pothandiza apolisi pa ntchito zolimbikitsa za chitetedzo cha mu m’dzinda-wu.

Mkulu mkuluyi m’chigawochi wanena izi pomwe amakumana ndi magulu a zachitetezo cha ku ma dera (Community Policing ) a m’boma la Zomba.

Iye wati akhala okondwa akamaona kuti anthu ambiri ochita za malonda monga amwenye ndi ena ambiri akumathandiza apolisi pa ntchito zawo monga powathandiza ndi mayendedwe ndi zina momwe anthu a zamalondawa akumachitira m’mizinda ina. raphael likaka analankhula ndi a mayi suwedi.

Posachedwapa mkulu wa apolisi-yu anakumana ndi kulimbikitsanso ubale wabwino pakati pa apolisi ndi makomiti a za chitetedzo cha ku madera m’bomalo. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875