Radio Maria Malawi lero lachisanu pa 13 May 2016 yayamba kuulutsa maprogramu amasiku atatu a Mariatona.
Kudzera m'maprogramuwa anthu akumapeleka thandizo lawo ku wailesiyi ndipo pakufuni ndalama zokwana 10 million kwacha kuti ikwanitse zina mwa ntchito zake monga kumanga Goloto,kulipira Macra license ndi kugula Back up power system.
↧