Pamene mariatona akupitira Radio Maria ikupempha anthu onse amene amakonda wailesiyi kupitira kutenga nawo ku maprogram wosiyana siyanasiyana komanso kupereka ndalama kudzera ma pledge Card amene akupedzeka madela wosiyana siyana.Ndalama imene ikusowekera ndi yokwana ten millione kwacha.
↧