Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Apempha Ansembe Alimbikitse Umodzi

Ansembe a mpingo wa katolika mu dayosizi ya Mangochi awapempha kuti alimbikitse umodzi pakati pawo ndi cholinga choti athe kutumikira bwino akhristu awo. Wachiwiri kwa wapampando wa bungwe la ansembe...

View Article


Ambuye Tambala Apempha a Misala Asataye Mtima

Episkopi wa dayosizi ya Zomba ya mpingo wakatolika Ambuye George Tambala wapempha anthu amene amadwala matenda a misala kuti asamakhale otaya mtima koma azikhala okhulupilira komanso okonda kupemphera....

View Article


Papa Wapempha Anthu a Mdziko la DRC Akhale Odezetsa Mtendere

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu a mdziko la Democratic Republic of Congo (DRC) kuti akhale okhululuka komanso odzetsa mtendere. Malinga ndi malipoti a...

View Article

WHO Ikhazikitsa Katemera wa Ebola Pofika 2018

Bungwe lowona za umoyo la World Health Organisation (WHO) lati pofika chaka cha 2018 likhala litakhazikitsa katemera woteteza anthu ku matenda a Ebola. Malipoti a wailesi ya BBC ati padakali pano...

View Article

Khirisimasi ndi Chikondwelero cha Kudzichepetsa kwa Mulungu-Papa

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wauza atsogoleri a mpingo kuti akuyenera kuzindikira kuti chikondwelero cha khrisimasi ndi nthawi yokondwelera kudzichepetsa kwa chikondi...

View Article


Papa Franscisco Apempha Achinyamata kuti Asabwelere Mmbuyo ndi Chikhulupiliro...

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wauza achinyamata kuti asalole wina aliyense awasochotsere mu chikhulupiliro chao mwa Mulungu. Malinga ndi uthenga omwe mtsogoleri wa...

View Article

Papa Francisco Wati Akhristu Akuyenera Kuyenda Mu Njira Ya Chiyembekezo.

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika-yu amalankhula izi ku likulu la mpingowu ku VATICAN pa mkumano omwe amakhala nawo lachitatu lililonse ndi anthu omwe amafika ndi kudzacheza ku likulu la mpingowu. Iye...

View Article

Nduna ya a Papa ku mayiko a Malawi ndi Zambia Imemeza Anthu Kuthandiza Radio...

Nduna ya a Papa m’mayiko a Malawi ndi Zambia , Arch-Bishop Julio Murat walimbikitsa akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti atenge umwini wothandiza Radio Maria chifukwa ndi chida chodalilika mu...

View Article


PMS iyamikira Mabungwe Amu Mpingo Wakatolika

Mabungwe osiyanasiyana mu mpingo wakatolika awayamikira kaamba ka ntchito yotamandika yomwe agwira mu mchaka cha 2016. Wapampando wa mabungwe a utumiki a apapa mdziko muno la Pontifical Missinaries...

View Article


Nduna ya a Papa ku mayiko a Malawi ndi Zambia Imemeza Anthu Kuthandiza Radio...

Nduna ya a Papa m’mayiko a Malawi ndi Zambia , Arch-Bishop Julio Murat walimbikitsa akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti atenge umwini wothandiza Radio Maria chifukwa ndi chida chodalilika mu...

View Article

Zigawenga za Islamic State Zavomera Kuti Zachita Chiwembu Mdziko la Turkey

Zigawenga za chisilamu za Islamic State ati ndi zomwe zachita chiwembu chomwe chaphetsa anthu 39 ndi kuvulaza ena pa malo ena achisangalalo mu mzinda wa Istanbul mdziko la Turkey. Zigawengazi ati...

View Article

Papa Adzudzula Mchitidwe wa Chiwembu Mdziko la Turkey

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco, wadzudzula mchitidwe wa chiwembu omwe wachitika mdziko la Turkey pomwe anthu 39 aphedwa ndipo ena 69 avulala pa malo ena achisangalo mu...

View Article

Matola Akukolezera Ngozi za Pansewu M’boma la Mangochi

Apolisi a pa nsewu mdziko muno adandaula kaamba ka kuchuluka kwa ngozi za pansewu m’boma la Mangochi. Mkulu wa apolisi a pansewu mdziko muno Assistant Commissioner Mcferson Matowe wauza Radio Maria...

View Article


Nduna ya a Papa ku mayiko a Malawi ndi Zambia Imemeza Anthu Kuthandiza Radio...

Nduna ya a Papa m’mayiko a Malawi ndi Zambia , Arch-Bishop Julio Murat walimbikitsa akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti atenge umwini wothandiza Radio Maria chifukwa ndi chida chodalilika mu...

View Article

Amayi a MpingoWakatolika Alimbikitsa Ubale Pakati Pawo

Amayi mpingo wakatolika kwa Chikapa mu Parish ya Nthawira mu arki dayosizi ya Blantyre awayamikira kamba kolimbikitsa ubale wabwino pakati pawo ndi amayi a  ku parish ya Chisitu ku Mulanje mu arki...

View Article


Radio Maria Mariatona 2016

Radio Maria Malawi mogwirizana ndi Ma Radio ena onse pa dziko lonse la pansi Mawa akuyamba ulendo wa masiku atatu umene umatchedwa kuti Mariatona, kuno ku Malawi ulendowu unayamba loweruka pa 7 May ku...

View Article

Akhristu Awalimbikitsa Kupeleaka Masika

Akhristu alimana la St .Joseph ku St.John Church m'parish ya Kausi mu Diocese ya Mangochi awalimbikitsa za ubwino wopeleka mowolowa manja pa miyambo yonse yochitika mu mpingowu. Bambo mfumu a parishiyi...

View Article


Maprogramu Amariatona

Radio Maria Malawi lero lachisanu pa 13 May 2016 yayamba kuulutsa maprogramu amasiku atatu a Mariatona. Kudzera m'maprogramuwa anthu akumapeleka thandizo lawo ku wailesiyi ndipo pakufuni ndalama...

View Article

Tsiku Lachiwiri Ulendo Wa Mariatona .

Pamene mariatona akupitira Radio Maria ikupempha anthu onse amene amakonda wailesiyi kupitira kutenga nawo ku maprogram wosiyana siyanasiyana komanso kupereka ndalama kudzera ma pledge Card amene...

View Article

Bwalo la Milandu Lilamula Anthu Asanu Kulipira 795,000 Kwacha

Bwalo lachiwiri la milandu m’boma la Machinga  lalamula amuna asanu ndi m’modzi 6 kuti alipire chindapusa cha ndalama zokwana 795,000 kwacha kulephera apo akakhale ku ndende kwa zaka zitatu atapezeka...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>