Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

CHIPANI CHA PPM CHIPIKISANA NAWO PA UPRESIDENT

$
0
0

Chipani cha People’s Progressive Movement PPM chati chidzapikisana nawo pa mpando wa Upresident pa  zisankho za chaka cha mawa kaamba koti chili ndi mfundo zake za tsopano zomwe zidzathandize pa chitukuko cha dziko lino.

President wa chipanichi Mark Katsonga Phiri ndi yemwe amalankhula izi lero pa msonkhaowu omwe chipanichi chinachititsa ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre. Katsonga Phiri wati ngakhale mmbuyomu chipanichi chakhala chikupanga mgwilizano ndi zipani zina, pakadali pano chapanga maganizo oti chidzapikisane nawo kaamba ka mfundo zomwe chilli nazo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>