OPHUNZIRA MSUKULU ZOSIYANASIYANA APHUNZITSIDWE ZA CHILENGEDWE
Unduna woona zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo wati ugwira ntchito ndi unduna wa zamaphunziro ndi cholinga choti ophunzira m’sukulu zosiyanasiyana aziphuzitsidwa mokwanira momwe angamasamalire...
View ArticleAkhristu ku America akukonda kwambiri Papa Francis
Kafukufuku wina yemwe akuluakulu ena achita m’dziko la America akuti akuwonetsa kuti akhristu ambiri a mpingo wa Katolika akukonda mtsogoleri wa mpingowu pa dziko lonse Papa Francis. Ngakhale kuti...
View ArticleBoma lipitiriza kulanda maukonde osavomerezeka kuphera nsomba ku Nyanja ya...
Boma lati lipitiriza kulimbikitsa kampeni yoteteza nsomba polanda maukonde osavomerezeka kuchokera kwa asodzi pofuna kuthana ndi mchitidwe wochita usodzi mosatsatira malamulo omwe ukuchititsa kuti...
View Article“Tidzidalire pa chitukuko” Bwanamkubwa.
Anthu m’boma la Mwanza awapempha kuti adzizidalira pantchito ndi cholinga chotukula miyoyo yawo komanso kupititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino. Bwanankubwa wa Bomalo a Gift Rapozo ndiomwe...
View ArticleBungwe la MEC latsutsa zoti likumayika zipangizo zosagwira bwino ntchito ku...
Bungwe lowona zachisankho la Malawi Electoral Commission MEC latsutsa malipoti oti likumayika zipangizo zosagwira bwino ntchito pa kalembera wa zisankho ku malo komwe anthu ena akuganiza kuti ndi komwe...
View ArticleMipingo ndi zipembedzo zakhazikitsa ndondomeko yothandiza kuti zisankho...
Magulu azipembedzo zosiyanasiyana mdziko muno atsekulira ntchito yomwe akuyitcha Interfaith Elections Initiative ngati njira imodzi yothandizira kuti zisankho za chaka cha mawa zidzayende bwino....
View ArticleOn 30th September we will know the canonisation date of the Popes- JOHN XXIII...
The Consistory will meet on Monday 30th September when Pope Francis will announce the canonization date for the two Pontiffs. Blessed John XXIII (aka Angelo Giuseppe Roncalli) was elected Pope on 28th...
View ArticleTHE POPE WILL PAY HOMAGE TO ST. FRANCIS
On 4th October this year, the day on which we remember the patron saint of Italy, Saint Francis, Pope Bergoglio will visit Assisi to pay homage to the place in which the son of the rich merchant Pietro...
View ArticleRadio Maria with the Pope for Peace
One of the cornerstones of the identity of Radio Maria is faithfulness to the Magisterium which becomes tangible not only in the editorial policy, but also in the special attention with which the key...
View ArticleCHIPANI CHA PPM CHIPIKISANA NAWO PA UPRESIDENT
Chipani cha People’s Progressive Movement PPM chati chidzapikisana nawo pa mpando wa Upresident pa zisankho za chaka cha mawa kaamba koti chili ndi mfundo zake za tsopano zomwe zidzathandize pa...
View ArticleOPHUNZIRA A VUTO LAKUSAWONA APEMPHA ZIPANGIZO ZA BRAIL KUTI ADZAVOTE BWINO.
Ophunzira omwe ali ndi vuto lakusawona pa sukulu ina m'boma la Mulanje apempha bungwe la Malawi Electoral Commission MEC kuti liwapititsire zipangizo za Brail kuti iwo adzathenso ku vota bwino pa...
View Article“Makhansala achepetsa ntchito za mafumu” T/A Nkangula
Sub T/A Nkangula ya m'boma la Zomba yati kusankhidwa kwa makhansala pa zisankho za chaka cha mawa kuthandiza kuchepetsa ntchito yomwe mafumu akhala akugwira zomwe zithandize pa chitukuko cha dziko...
View ArticleBUNGWE LA MEC LIDZITSEKULANSO MALO AKALEMBERA ENA PAKAKHALA MAVUTO ENA
Bungwe lowona za chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lati litsekulanso malo ena olembetsera kalembera wa zisankho ku malo omwe anthu sanathe kulembetsa kwa masiku 14 kamba ka mavuto ena....
View ArticleZIWONETSERO ZOKWIYA NDI BOMA MUMZINDA WA BLANTYRE
Pamene kwangotsala miyezi yowerengeka kuti dziko lino lichititse chisankho cha pulezidenti mabungwe omwe siaboma pansi pa mgwirizano wawo olimbikitsa nkhani za demokalase ndi ulamuliro wabwino mdziko...
View ArticleMAPHUNZIRO A MAWU A MULUNGU A LERO
Kukhala maphunziro kwa onse amene amawerenga Mawu a Mulungu a lero pa Radio Maria ku Limbe Cathedral ku Blanyre loweruka pa 1 March 2014 nthawi ya 8 koloko mmawa. Pobwera atenge zinthu izi, Baibulo,...
View ArticleOPHUNZIRA AM'SUKULU ZASEKONDALE APINDULA NDI DSTV
Kampani ya Multi Choice Malawi yati ophunzira a m’sukulu zasekondale zomwe sizaboma tsopano ali ndi mwayi opindula nawo kudzera ku mapologalamu awulele othandiza pamaphunziro omwe amawonetsedwa pa...
View ArticleANTHU AKU CHIKHWAWA AKUKAKAMIZA MFUMU YAWO KUTI ITULE PANSI UDINDO
Anthu a mdera la mfumu Ngowe m’boma la Chikhwawa awopseza kuti achita ziwawa ngati boma siliwathandiza pa nkangano wawo ndi mfumu Ngowe yomwe ati yakhala ikugulitsa minda yawo kwa anthu andale komanso...
View ArticleBAMBO APEZEKA NDI MAFUPA A MUNTHU KU MANGOCHI
Bwalo la magistrate ku Namwera mboma la Mangochi lalamula mzika ya zaka 37 ya mdziko la Mozambique, Jairosi Duwa kukakhala kundende chifukwa chopezeka ikugulitsa mafupa a munthu kwa munthu wina...
View Article92 BILIYONI KWACHA INABEDWA MCHAKA CHA 2010-JB
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Joyce Banda wati kafukufuku wapeza kuti ndalama pafupifupi 92 biliyoni kwacha za boma zinasowa m'chaka cha 2010 mu ulamuliro wachipani cha Democratic Progressive (DPP)....
View ArticleNDUNA YA ZA UMOYO YATI KUNYALANYAZA KWA OGWIRA NTCHITO KUNAWONGETSA MATUPI A...
Nduna ya za umoyo mayi Catherine Gotani Hara, ati kunyalanyaza kwa akulu akulu apachipatala cha Kamuzu Central mu mzinda wa Lilongwe ndi komwe kunachititsa kuti matupi ochuluka a anthu awonongeke ku...
View Article