Quantcast
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mphepo ya Mphamvu Ichititsa Anthu 45,000 Kusowa Pokhala

Mphepo ya mkuntho komanso ya mphamvu yaononga nyumba za anthu ndikusiya mabanja okwana 45,000 alibe malo okhala mu mzinda wa Queensland mdziko la Australia.

Malipoti a wailesi ya BBC ati nduna yaikulu ya mdzikolo a Malcolm Turnbull yalamula anthuwo kuti achoke kumalo wa omwe ati akuika miyoyo ya anthuwo pa chiopsezo chachikulu. M’chaka cha 2011, anthu oposa 25,000 a m’derali adapemphedwa kuti achoke ku malowo posatila mphepo ya ngati yomwe-yi imene inachitikanso m’chakacho. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>