Akagwira Jere Zaka 9 Kamba Ka Kuba
Bwalo la milandu m’boma la Mangochi lalamula mamuna wina wa zaka 28 zakubadwa kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka zisanu ndi zinayi litamupeza olakwa pa mlandu...
View ArticlePapa Avomereza Fancisko ndi Yasinta Odala Kukhala Oyera
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wavomereza kuti Francisco ndi Yacinta Odala a mdziko la Portugal ana omwe anakumana ndi Mai Maria wa ku Fatima atchulidwe oyera. Malinga...
View ArticleMphepo ya Mphamvu Ichititsa Anthu 45,000 Kusowa Pokhala
Mphepo ya mkuntho komanso ya mphamvu yaononga nyumba za anthu ndikusiya mabanja okwana 45,000 alibe malo okhala mu mzinda wa Queensland mdziko la Australia. Malipoti a wailesi ya BBC ati nduna yaikulu...
View ArticleBoma Likhutira ndi Radio Maria Malawi
Boma lati ndi lokhutira ndi momwe Radio Maria Malawi ikugwilira ntchito zake. Nduna ya zofalitsa nkhani yomwenso ndi mneneri wa boma wolemekezeka a Nicholus Dausi ndi omwe anena izi pamene anayendera...
View ArticleAkagwira Ukayidi Kamba Kogwilira Ana Awiri
Bwalo la milandu la Mkukula Magistrate mu mzinda wa Lilongwe lalamula bambo wina kuti akakhale ku ndende kwa zaka zisanu ndi zitatu (8) ndikukagwira ntchito yakalavula gaga atamupeza olakwa pa mlandu...
View ArticleKathrada Wamwalira
Yemwe anali mtsogoleri pothetsa mchitidwe wa tsankho mdziko la South Africa a Ahmed Kathrada wamwalira. Malipoti a wailesi ya BBC ati a Kathrada amwalira ali ndi zaka 87 zakubadwa, atadwala kwa...
View ArticleBungwe la LEAD Lakwanitsa Kubwezeretsa Chilengedwe Mchigwa cha Nyanja ya Chilwa
Boma lati bungwe la Leadership for Environment and Development in Southern and Eastern Africa (LEAD-SEA) lakwaniritsa ntchito yake yolimbikitsa ndi kubwezeretsa chilengedwe mchigwa cha Nyanja ya Chilwa...
View ArticleKhosolo ya Zomba Ichita Mgwirizano ndi Changalume Barracks
Khonsolo ya mzinda wa Zomba yakhazikitsa ubale ndi gulu la asilikali a nkhondo aku Changalume Barracks. Polankhula pa mwambo wosayinilana ubale-wu omwe unachitikira ku likulu la khonsolo-yi, Mayor wa...
View ArticleMEC Ikukonzanso Malire a Madera Olowana
Bungwe lowona za chisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lapempha aphungu akunyumba ya malamulo komanso ma khansala kuti akanene ku bungweli ngati malire a mdera lawo alowelelana ndi...
View ArticleApempha Atolankhani Alondoloze Thumba la Ndalama za Sukulu za Boma
Bungwe la achinyamata la Youth InitiativeforCommunity Development(YICOD) lati atolankhani ali ndi udindo wofalitsa nkhani zokhudza momwe ndondomeko ya ndalama za m’thumba la sukulu za boma la School...
View ArticleAnthu Azisunga Agalu Osaposera Atatu Kuti Apewe Chiwewe
Matenda a chiwewe akuti angathe ngati anthu atamakhala ndi agalu osachepera atatu m’makomo mwawo. M’modzi mwa akuluakulu kuofesi yoona za nyama ya Vetenale ku Thondwe m’boma la Zomba a William...
View ArticleMafumu a Mizinda Mdziko la Rwanda Alamulidwa Kukakhala Kundende Moyo Wawo Wonse
Bwalo la milandu m’dziko la France lalamula mafumu awiri a mizinda ina ya m’dziko la Rwanda kuti akakhale kundende moyo wawo wonse kamba kokhudzidwa ndi mulandu wakuphedwa kwa anthu ochuluka m’chaka...
View ArticleDayosizi ya Chikwawa Ipempha Thandizo la Chakudya
Dayosizi ya mpingo wa katolika Chikwawayapempha anthu komanso mabungweakufuna kwabwino kuti athandize anthu okhala m’dera la kunsi kwa m’tsinje wa Shire omwe akhudzidwa kwambiri ndi mavuto a njala....
View ArticlePapa Apempha Anthu Asamalire Anthu Othawa Kwawo
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko wati mayiko akuyenera kusamalira bwino anthu omwe akumafika m’mayiko awo kamba kothawa nkhondo ndi zipolowe zomwe zikuchitika m’mayiko...
View ArticleMayiko Achilimike Pothetsa Mchitidwe Wozembetsa Anthu-Papa
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ntchito yolimbana ndi m’chitidwe wozembetsa anthu itha kukhala yopanda pake ngati mayiko sazichilimika pa ntchito yolimbana ndi...
View ArticleApolisi Amanga Anthu 20 ku Mchinji
Anthu makumi awiri (20) ali m’manja mwa apolisi m’boma la Ntchisi kaamba kowaganizira kuti apalamula milandu yosiyanasiyana. Malingana ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Sergeant Gladson...
View ArticleAnthu 8 Afa pa Chipolowe Mdziko la India
Anthu asanu ndi atatu 8 afa ndipo ena ambiri avulala pa chipolowe chomwe chinabuka pakati pa apolisi ndi anthu ena omwe amachita ziwonetsero pa chisankho cha padera mdziko la India. Malipoti a wailesi...
View ArticlePapa Wadzudzula Chiwembu cha Matchalitchi a Anglican Mdziko la Egypt
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse PapaFancisko wadzudzula chiwembu chomwe chachitika m’matchalitchi awiri a mpingo wa Anglican mu mzinda wa Cairo mdziko la Egypt chomwe chapha anthu 44...
View ArticleApolisi Akusakasaka Dalaivala Wina Kaamba Kopha Munthu, Kuthawa
Apolisi m’boma la m’boma laDowaakufunafuna dalaivala wa galimoto ina kamba komuganizira kuti anagunda ndi kupha a Akimu Dayison a zaka 38zakubadwa m’bomalo. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant...
View ArticleAnthu 20 Afa Boti Litamira Mdziko la Myanmar
Anthumakumi awiri (20)afa boti lomwe anakwera litaombana ndi linzake ndi kumira mu m’tsinje wina m’dziko la Myanmar. Malingana ndi malipoti a News 24 anthu amene anali mu botili ndi oti anali...
View Article