Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Dinale Ya Mangochi Idzipereka Pa Utumiki Wa Ana

$
0
0

Dinale ya Mangochi mu mpingo wakatolika yati idzipeleka pa ntchito yolimbikitsa ntchito za utumiki wa ana.

Sister Marita Tepelo achipani cha Devine Providence otumikira mu dinaleyi ndi omwe anena izi potsatira maphunzuro omwe atsogoleri a bungwe la za utumiki wa ana m’dziko muno anachita posachedwapa mu m’nzinda wa Lilongwe. Iwo ati kudzera m’ma phunzirowo dinale ya Mangochi yakonza mapulani oti ithandizenso anthu ena kudziwa za kasamalilidwe kabwino ka ana mu mpingo ndi kuthandziza anawo kuzindikila za chiyitanidwe chawo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>