Dinale Ya Mangochi Idzipereka Pa Utumiki Wa Ana
Dinale ya Mangochi mu mpingo wakatolika yati idzipeleka pa ntchito yolimbikitsa ntchito za utumiki wa ana. Sister Marita Tepelo achipani cha Devine Providence otumikira mu dinaleyi ndi omwe anena izi...
View ArticleZigawenga za IS Zagonjetsedwa
Asilikali a mdziko la Iraq ati ali kumapeto kwa ntchito yogonjetsa zigawenga zachisilamu za Islamic State zomwe zinakhazikika mu mzinda wa Mosul mdzikolo kuyambira mu chaka cha 2014. Malinga ndi...
View ArticlePapa Akumbutsa Makadinala Atsopano Ntchito Yawo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco walimbikitsa makadinala asanu omwe wangowadzoza kumene kuti ntchito yao ndi kutumikira akhristu. Papa amalankhula izi ku likulu la mpingowu...
View ArticleAnthu Anayi Afa Pa Ngozi Ya Galimoto
Anthu anayi afa ndipo ena avulala modetsa nkhawa pa ngozi ya galimoto zomwe zinaombana m’boma la Dowa. Malinga ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergent Richard Kaponda ngoziyi yachitikira...
View ArticleApempha Akhristu Kupemphelera Mtendere ndi Mgwirizano
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu pa dziko lonse kuti apemphelere mtendere ndi mgwirizano m’dziko la Venezuela. Papa amalankhula izi ku likulu la mpingowu...
View ArticleBambo Wina Wapha Mkazi Wake Kaamba Ka Nsanje.
Apolisi ku Kanengo mu m’zinda wa Lilongwe akusunga m’chitolokosi bambo wina wa dzaka 36 zakubadwa kamba komuganizira kuti anamenya ndikupha mkazi wake. Ofalitsa nkhani za apolisi ku delaro Sergeant...
View ArticleAkhristu Apemphedwa kutengapo Mbali Mu Mpingo Wa Katolika
Akhristu a mpingo wa katolika awapempha kuti azilimbikitsa magulu osiyanasiyana amu mpingo-wu ngati njira imodzi yopititsira patsogolo moyo wachipembedzo mu mpingo. Wapampando opuma ku tchalichi la St...
View ArticleBoma la Balaka Lichita Tsiku Loganizira Mwana wa ku Africa
Makolo ati ali ndi udindo wolimbikitsa ufulu wa ana powonetsetsa kuti ufulu wao wa maphunziro ndi maufulu ena akukwaniritsidwa. Bwanamkubwa wa boma la Balaka a Rodrick Mateauma ndi omwe alankhula izi...
View ArticleMnyamata Afa Ndi Ngozi Ya Moto
Mnyamata wina wafa pa ngozi ya moto wa petulo umene unabuka mu golosale yake yomwe inali pa msika wa Chisamba m’boma la Ntchisi. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Gladson Mbumpha...
View ArticleAnthu makumi Asanu Amira pa Nyanja ya Meditteranean
Bwato lomwe linanyamula anthu oposa makumi asanu akuliganizira kuti lamira pa nyanja yaikulu ya Meditteranean mdziko la Morocco. Malinga ndi malipoti a bbc magulu opulumutsa anthu pa ngozi za pa madzi...
View ArticleAnthu Apewe Kusankhana Mitundu
M’tsogoleri wa dziko lino Professor Peter Muthalika wapempha anthu m’dziko muno kuti azipewa kusankhana mitundu kamba koti izi sizingathandize pa chitukuko cha dziko lino. President Muthalika wanena...
View ArticleSister Maloya a Chipani cha SBVM Ayikidwa Mmanda
Mwambo woika m’manda thupi la malemu sister Patricia Maloya chipani cha Atumiki a Maria Virigo Woyera uchitika lero ku Maryview ku Nguludi m’boma la Chiradzulu. Malinga ndi a ku likulu la chipani-chi...
View ArticleMafumu Ati Adzigwira Ntchito Limodzi ndi Boma
Mfumu yayikulu Mbenje ya m’boma la Nsanje yalangiza mafumu m’dziko muno kuti adzigwira ntchito limodzi ndi boma lomwe likulamula ndi cholinga chofuna kulimbikitsa ntchito za chitukuko m’dziko lino....
View ArticleApempha Akhristu Kukhala Chitsanzo Chabwino
Akhristu a m’phakati wa St Peters ku parish ya Sacred Heart mu dayosizi ya Zomba awalangiza kuti akhale chitsanzo chabwino komanso olimba pa chikhulupiliro chawo potengera momwe nkhoswe ya mphakati...
View ArticleBambo Simon Nyalugwe Alowa M’manda
Mwambo woyika m’manda thupi la malemu bambo Simon Nyalugwe omwe amatumikira ku dayosizi ya mpingo wakatolika ya Zomba wachitika lolemba pa 22 August 2016ku Zomba Cathedral mu dayosizi ya Zomba. Malinga...
View ArticleMpingo Wakatolika Mdziko Muno ati Udzapindula ndi Msokhano wa WUCWO
Mpingo wakatolika mdziko muno akuti udzapindula kwambiri ndi msonkhano wa bungwe la amayi achikatolika pa dziko lonse waWorld Union of Catholic Women Organisation(WUCWO)umene awukonza kuti uchitikire...
View ArticleAlimbikitsa Anthu Kuganizira za Chitukuko cha Dziko Lino
Wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino Dr Saulos Chilima wati nkofunika kuti anthu m’dziko muno ayambe kuganiza mwakuya ndi kupeza njira zabwino zomwe zingathandize pa ntchito zotukula dziko lino....
View ArticleApempha Ansembe Kudzipereka pa Utumiki Wawo
Ansembe mu dayosizi ya Mangochi awapempha kuti akhale odzipereka pa utumuki wawo komanso adzisamalira katundu osiyanasiyana yemwe amagwiritsa ntchito. Polankhula pambuyo pa msulo wa ansembe omwe...
View ArticleMigwirizano Ina Ikhumudwitsa Papa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndi wokhumudwa ndi migwirizano yomwe imakhalapo pakati pa maiko omwe ndi amphamvu komanso otukuka pa chuma. Papa Francisco wati...
View ArticleNtchito Yolimbana ndi Mbozi ati Ikuyenda Bwino
Boma lati ntchito yolimbikitsa kuthana ndi mbozi zachilendo zofanana ndi ntchembele zandonda zomwe zagwa mdziko muno ikuyenda bwino. Dr. Godfrey Ching’oma omwe ndi mlangizi wamkulu woona za mbewu mu...
View Article