Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Apempha Mafumu Kukhale Tchelu Pa Nthawi Yovota

$
0
0

Mafumu a m’boma la Nsanje awapempha kuti awonetsetse kuti anthu omwe azavote nawo pa chisankho cha chibweleza chomwe chikuyenera kudzachitika m’dera la Nsanje Lalanje ndi okhawo amene ndi ochokera m’derali.

M’modzi mwa akuluakulu a bungwe loona za chisankho m’dziko muno a Issack ndi omwe anena izi pomwe amakumana ndi mafumu a m’dera la mfumu yayikulu Mbenje m’bomalo.  

Iwo ati mafumu mdziko muno akuyenera kuonetsetsa kuti anthu a kumadera ena sakufika ndi kudzalembetsa nawo mayina awo mkaundula wa chisankho chapadera chomwe chikhale chikutika m’ma dera ena m’dziko muno


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>