M’nyamata Wina Ku Mangochi Atema Ndi Kupha Anthu Awiri.
Mnyamata wina wa zaka 25 zakubadwa ali m’manja mwa apolisi m’boma la Mangochi kamba komuganizira kuti wapha mkazi wake wakale kuphatikizaponso apongozi ake . Apolisi ku Monkebay m’boma la Mangochi ndi...
View ArticleAyamikira Makolo Poonetsa Chidwi Pa maphunziro A Atsikana
Makolo omwe ana awo amaphunzira pa sukulu ya pulayimale ya St John m’boma la Mangochi awayamikira kamba kodzipeleka pa ntchito zotukula maphunziro a atsikana pa sukulu-yi. M’phunzitsi wa mkulu pa...
View ArticleAmayi Awapempha Kuti Azithandiza Amayi Anzawo Ovutika.
Amayi a mpingo wakatolika awapempha kuti adzipereke pa ntchito yothandiza amayi anzawo omwe akukomana ndi mavuto osiyanasiyana m’dziko muno. Mkazi wa wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino , mayi Mary...
View ArticleAchinyamata Amanga Malo A Sikero Ku Chipatala Cha Thondwe.
Akuluakulu a chipatala cha Thondwe m’boma la Zomba ayamikira bungwe la achinyamata la Mwana Wa M’mudzi chifukwa chomanga malo asikelo ya ana pa chipatalacho. Mkulu wa alangizi a za umoyo ku Thondwe a...
View ArticleBungwe La CWO Ku Mangochi Lichita Msonkhano Wake Wa Pa Chaka.
Msonkhano wa bungwe la amayi achikatolika mu dayosizi ya Mangochi wa chaka chino unayamba pa 17 August ndikutha pa 20 august 2017. Amayi ochokera m’ma dinale onse opezeka mu dayosiziyi ndi omwe atenga...
View ArticleNtchito Zokweza Amayi Sizikuyenda Bwino Ku Lilongwe
Ntchito yopeleka luso losiyanasiyana pakati pa amayi mu mpingo wakatolika mu arch-dayosizi ya Lilongwe akuti ikukomana ndi mavuto osiyanasiyana. Bambo Francis Lekaleka , omwe ndi bambo mlangizi wa...
View ArticleAzuzula Anthu Kaamba Ka Mauthenga Aboza
M’tsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (Mcp) Dr Lazarus Chakwera , wadzudzula anthu ena omwe akuti akufalitsa mauthenga ofuna kugawanitsa anthu pa nkhani za chipembedzo m’dziko muno. Dr Chakwera...
View ArticleAchinyamata Awapempha Kukhala Omasuka Pofotokoza Nkhawa Zawo.
Mpingo wakatolika m‘dziko muno wapempha achinyamata kuti azikhala omasuka pofotokozera mpingo, pa zamavuto omwe amakhala akukomana nawo. Mlembi wa mkulu , ku likulu , la mpingo wakatolika mdziko muno,...
View ArticleAlimbikitsa Akhristu Kulandira Masacramenti
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awalimbikitsa kuti azikonda kulemekeza Sacrament la Ukaristia kamba koti sacramentili ndi limodzi mwa ma sacrament opamba pakati pa akhristu mu mpingowu. Bambo...
View ArticleEpiskopi Apempha Akhristu Apite ku Malo Oyera Chaka cha Chifundo Chisanathe
Episkopi wa dayosizi ya mpingo wakatolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima apempha akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti chaka cha jubilee ya chifundo cha Mulungu chisanathe apite ku malo...
View ArticleChilima Apempha Akhristu Agule New Catholic Answer Bible
Akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno awapempha kuti agule baibulo la tsopano la mpingowu lomwe akulitcha New Catholic Answer Bible ndi cholinga choti azame mu chikhulupiliro chawo komanso...
View ArticleAnthu Atatu Afa pa Ngozi ya pa Shoprite
Chiwerengero cha anthu omwe afa pa ngozi yomwe yachitikadzulopa Shoprite mu msewu wa Masauko-Chipembere mu mzinda wa Blantyreakuti chafika pa atatu. Ngoziyi yachitika dzuro cha ku m’mawa, galimoto la...
View ArticleDayosizi Ya Mangochi Yakonza Msonkhano Wofunika Kwambiri.
Msonkhano waukulu wokonzekera tsiku la nkhoswe ya dayosizi ya Mangochi akuti udzachitika loweluka likudzali pa 26 August 2017 ku likulu la dayosizi-yi ku Mangochi. Akulikulu la dayosizi-yi ndi omwe...
View ArticleMsonkhano Wa Transformation Alliance Uchitikira Ku St Pius Catholic Hall
Gulu la anthu a ndale la Trasformation Alliance lati tsopano lapeza malo atsopano ochitilako m’sonkhano wake waukulu. Ofalitsa nkhani za guluri a Leonard Chimbaka wati guluri tsopano lapeza malo mu...
View ArticleAwalimbikitsa Kupitiliza Ntchito Yotumikira Radio Maria Malawi
Otumikira Radio Maria Malawi ku Zomba awalimbikitsa kuti asafooke koma kuti adzidzipeleka pa ntchito yawo. Bambo Peter Lufeyo, otumikira mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba ndi omwe anena izi...
View ArticleAwalimbikitsa Kuti Akalembetse Mkaundula Wa Umzika
Anthu a m’boma la Zomba awalimbikitsa kuti asanyozere koma kuti akalembetse mayina awo mkaundula wa ziphatso za umzika. Mkulu wa mu ofesi ya bwana mkumbwa pa nkhani za zakalembera a Tobias Lutepo ati...
View ArticleKomiti Yaku Parliament yoona za misewu Iyendera Msewu Wa Chingale.
Anthu a m’madera a mmaboma a Zomba, Machinga ndi Blantyre ati ndiokondwa kaamba ka kubwera kwa komiti yowona za misewu ya kunyumba ya malamulo yomwe inakayendera msewu wa Chingale umene wadutsira m’ma...
View ArticleApempha Mafumu Kukhale Tchelu Pa Nthawi Yovota
Mafumu a m’boma la Nsanje awapempha kuti awonetsetse kuti anthu omwe azavote nawo pa chisankho cha chibweleza chomwe chikuyenera kudzachitika m’dera la Nsanje Lalanje ndi okhawo amene ndi ochokera...
View ArticleAtolankhani ali ndi Udindo Wodziwa za Kadyedwe Kabwino
Boma lati atolankhani m’dziko muno ali ndi udindo wodziwa za kadyedwe kabwino kaamba koti ndi anthu omwe amafalitsa mauthenga mosavuta. Mlangizi wamkulu wowona za kadyedwe kabwino, HIV ndi edzi mu...
View ArticleApolisi Akufunafuna Anthu Amene Afukula Manda M’boma la Machinga
Apolisi m’boma la Machinga ati akufunafuna anthu ena omwe sakudziwika omwe afukula manda m’mudzi mwa Chinguwo kwa Sub TA Mchiguza m’bomali. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Constable DavieSulumba...
View Article