Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Anthu mdziko muno awapempha kuti adzipeleke Posamalira Zachilengedwe.

$
0
0

Boma lapempha anthu kuti adzipeleke pa ntchito zotetedza ndikusamalira zachilengedwe , kamba koti izi zingathandizenso pa ntchito zokopa alendo m’dziko muno.

Mkulu owona za chuma ku unduna wa zamalonda ndi ma fakitale a Joseph Mkandawire , ndi omwe anena izi lachitatu , pa 27 September 2017 , ngati mlendo wolemekezeka pa mwambo wokumbukira nkhani zokopa alendo m’dziko muno , womwe unachitikira pa bwalo la zamasewero la Gynkana m’boma la Zomba.  

Iwo ati ngati dziko la Malawi lingamachite bwino pa nkhani yotetedza zachilengedwe ndiye kuti izi zithana kuthandiza kuti dziko lino likhala lachikoka pa ntchito zokopa alendo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>