Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Boma la Malawi Lati Liyesetsa Pothana ndi vuto La Kuthimathima Kwa Magetsi

Boma la Malawi lati likuyesetsa pa ntchito yolimbana ndi vuto lakuthimathima kwa magetsi lomwe likupitilirabe kuchitika m’dziko muno. Nduna yoona zachilengedwe, magetsi ndi migodi  olemekezeka a Aggrey...

View Article


Ngozi za pa Nsewu Zachepa ndi 39 Percent

Ngozi za pansewu m’dziko muno akuti zachepa ndi 39 percent m’miyezi isanu ndi inayi 9 yapitayi poyerekeza ndi nthawi ngati yomweyi chaka chatha. Wofalitsa nkhani za apolisi mdziko muno a James...

View Article


Akayidi 170 Athawa ku Ndende Mdziko la Haiti

Akaidi oposa 1 hundred 70 athawa mu ndende ina kumpoto kwa dziko la Haiti. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, akaidi omwe athawawo ati aba mfuti zisanu ndi kupha mulonda m’modzi wa pa malowa...

View Article

SACCO Yapereka Zipangizo ku Chipatala cha Dedza

  Bungwe la aphunzitsi losunga ndi kubwereketsa ndalama la SACCO m’chigawo cha pakati lapereka zipangizo zogwiritsa ntchito pa chipatala cha boma la Dedza.   Malinga ndi wamkulu wa bungweli a Henry...

View Article

Radio Maria Malawi itsekera masiku atatu a Mariatona Kathithi

Radio Maria Malawi yatsekera masiku atatu a Mariatona wa kathithi.   Malinga ndi m'modzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za wailesiyi a Emmanuel Kaliati, mariatona kathithiyu atsekeleredwa ndi mwambo...

View Article


Mayi Kajawo Ati ndi okondwa ndi thandizzo la M’thenda Ya Mtima Lomwe Mwana...

Makolo a m’sungwana yemwe wakhala akuvutika ndi mthenda ya mtima ati ndiokondwa kaamba ka thandizo lamphamvu lomwe mwana wawo walandira mdziko la Italy. Polankhula ndi Radio Maria Malawi Mai Catherine...

View Article

Ambuye Tambala Apempha Akhristu Kuti Agwirane Manja Potumikira Mpingo.

Mkulu owona zofalitsa nkhani , mauthega ndi kafuku-fuku ku bungwe la ma episikopi a mpingo wa katolika m’dziko muno laEpiscopal Conference Of Malawi (ECM) Ambuye George Desmond Tambalaapempha akhristu...

View Article

Awapempha Kuti Adzipereke Pa Ntchito Zokweza Dayosizi Yawo.

Mpingo wakatolika mu Arch-Diocese ya Blantyre wapempha akhristu ake kuti ayendere limodzi ndi atumiki awo padongosolo lokonzanso masomphenya a mmene dayosiziyi iyendere zaka zisanu zikubwerazi. Bambo...

View Article


School ya Sekondale ya Thondwe yalandira mphatso ya Ma Computer 34

Bungwe la COMPUTERS FOR MALAWI SCHOOLS lapeleka maComputer okwana (34) pa Sukulu ya Sekondale ya St Anthony ku THONDWE m’boma la Zomba. Polandira katunduyu mkulu wazamaphunziro a Mc Gregory Alfandika...

View Article


Mpempho Yamphamvu Isasula Nyumba Zawo

Maanja pafupifupi khumi ndi asanu(15) akusowa pokhala nyumba zawo zitasasuka ndi mphepo yamphamvu mdera la Nswaswa kwa Mfumu yaikulu Mlumbe m’boma la Zomba.   Khansala wa delari a GANIZANI MALISHE...

View Article

Radio Maria Malawi itsekera masiku atatu a Mariatona Kathithi

Radio Maria Malawi yatsekera masiku atatu a Mariatona wa kathithi.   Malinga ndi m'modzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za wailesiyi a Emmanuel Kaliati, mariatona kathithiyu atsekeleredwa ndi mwambo...

View Article

Akhristu a Parish ya Thondwe Athandiza Chipatala cha Zomba

Akhristu a mpingo wa katolika mu parishi ya St. Anthony Thondwe apereka thandizo la katundu wosiyanasiyana kwa odwala a pa chipatala chachikulu cha boma la Zomba. Malinga ndi bambo mfumu a parishiyi...

View Article

Boma Lipempha Anamwino Agwire Ntchito Modzipereka

Boma lapempha anamwino mdziko muno kuti azigwira ntchito yawo molimbika, mokhulupilika komanso modzipereka. Nduna ya zaumoyo Dr. Peter Kumpalume apereka pempholi pa mwambo wopereka ma diploma ndi ma...

View Article


Awapempha Kuti Akhale Ndi Chidwi Chofalitsa Uthenga Wabwino Wa Mulungu.

Akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno awapempha kuti akhale ndi chidwi chofalitsa uthenga wabwino wa mulungu. Mkulu wa mu ofesi yoona za mabungwe a utumiki wa apapa la Pontifical Mission Societies...

View Article

Papa Francisco Wayamikira Ansembe Anayi A Mziko La United States Of America.

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco wayamikira ansembe anayi omwe achita bwino pa mpikitsano wa ophunzira a msukulu za ukachenjede zomwe akhala akuphunzira m’dziko la United...

View Article


Anthu mdziko muno awapempha kuti adzipeleke Posamalira Zachilengedwe.

Boma lapempha anthu kuti adzipeleke pa ntchito zotetedza ndikusamalira zachilengedwe , kamba koti izi zingathandizenso pa ntchito zokopa alendo m’dziko muno. Mkulu owona za chuma ku unduna wa zamalonda...

View Article

Apapa Franciso Alandira Bwino Anthu Othawa Kwawo Omwe Afika Ku Vatican

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco, walandira anthu othawa nkhondo ochokera m’mayiko osiyanasiyana amene afika ku likulu la mpingo-wu ku vatican. papa francisco , walandira...

View Article


Papa Francisco Afunila Zabwino Ma Episikopi Aku Ulaya

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko  lonse Papa Francisco wafunila zabwino ma episikopi a mpingo wakatolika ochokera m’mayiko a ku ulaya la Council Of European Bishops' Conferences , omwe ali...

View Article

Bungwe La Mub Liyamikira Banki Yayikulu Mdziko Muno Ya Reserve

Bungwe la Malawi Union of the Blind (MUB) layamikira bank yayikulu ya Reserve, kamba koyika chidwi pa ntchito yoonetsetsa kuti anthu omwe ali ndi mavuto a kusaona azitha kulandira bwino mauthenga...

View Article

Anthu Apha Mfumu Yayo Mboma La Nsanje.

Anthu olusa a m’mudzi mwa chidzenga m’dera la mfumu yaikuklu Mlolo m’boma la Nsanje lachinayi awotcha ndikupha Nyakwawa yawo kaamba koiganizira kuti imagwilizana ndi anthu opopa magazi m’delaro....

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>