Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Papa Achita Mkumano ndi Akulu Akulu a Zipembedzo Mdziko la Iraq

$
0
0

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ati anachita mkumano ndi akuluakulu owona za chikhalidwe cha chipembedzo cha chisilamu komanso owona za ubale a mipingo ya chikhristu a m’dziko la Iran.

Pa msonkhanowu Papa anayamikira anthu onse omwe anafika ku ochokera mdziko la Iran ndipo wati msonkhanowu omwe uli wa khumi chiyambireni misonkhano ya mtunduwu ndi ofunika kwambiri.

Malipoti a wailesi ya Vatican ati pamsonkhonowu akuluakuluwa akambirana za zamtopola zomwe magulu osiyanasiyana amachita mu dzina la chipembedzo.

Pamenepa Papa wauza akuluakuluwa kuti onse pamodzi akuyenera kupeza njira zothetsera mchitidwe wa mtunduwu.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>