Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Apempha Boma Kulowererapo Pankhani Yakusowa Kwa Magetsi msukulu za Sekondare...

Vuto la kusowa kwa magetsi m’sukulu za ku midzi akuti ndi limene likukoledzera mavuto a kusachita bwino pakati pa ophunzira m’sukuluzi pa maphunziro awo. Wachiwiri kwa m’phunzitsi wa mkulu pa sukulu ya...

View Article


Galimoto Lapsa M’boma la Dowa

Galimoto la mtundu wa truck m’boma la Dowa ati lapsa potsatira ngozi yomwe galimotoli lachita pafupi ndi msika wa Chakhungu m’bomalo. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali SergeantRichard...

View Article


Anthu 142 Avulala pa Ngozi ya Sitima Mdziko la India

Anthu 142 ati afa ndipo ena oposa 200 avulala stima ya pa mtunda yomwe anakwera itachita ngozi mu mzinda wa Pradesh kumpoto kwa dziko la India. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBCanthu pafupifupi 58...

View Article

Anthu 73 Afa Mdziko la Mozambique

Anthu pafupifupi 73 akuti afa ndipo ena 160 avulula mdziko la Mozambique potsatira ngozi la galimoto la mtundu  Truck lomwe laphulika litanyamula mafuta. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC ngoziyi...

View Article

Apolisi Mchigawo cha ku M’mwawa Alonjeza Kupereka Chitetezo Chokwanira

Apolisi mchigawo cha kummawa kwa dziko lino ati akuchita chotheka kuwonetsetsa kuti anthu mchigawochi akulandira chitetezo chokwanira. Wofalitsa nkhani za apolisi mchigawochi Inspector Joseph...

View Article


Bungwe la AU Lati Asilikali a Dziko la Zimbabwe “Alanda Boma”

Bungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa la African Union (AU), lati zomwe achita asilikali a dziko la Zimbabwe potenga udindo oyendetsa boma, ndi chimodzimodzi kulanda boma ngakhale asilikaliwo...

View Article

Ma Episkopi Agwirizana ndi Mfundo za AU, EU

Maepiskopi a mpingo wa katolika mmaiko a Africa ndi ku Ulaya, ayamikira mfundo zomwe bungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa ndi ulaya, agwirizana kuti adzakambirane, pa msonkhano wawo wachisanu omwe...

View Article

Apolisi Akusaka Dalaivala Yemwe Wapha Munthu ndi Kuthawa

Apolisi m’boma la Ntchisi akufunafuna oyendetsa galimoto wina yemwe wapha munthu atamuwomba ndi galimoto ndikuthawa.       Malinga ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant Gladson M’bumpha,...

View Article


Papa Achita Mkumano ndi Akulu Akulu a Zipembedzo Mdziko la Iraq

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ati anachita mkumano ndi akuluakulu owona za chikhalidwe cha chipembedzo cha chisilamu komanso owona za ubale a mipingo ya chikhristu a...

View Article


Chipani cha Democrat Mdziko la America Chikufuna Mavoti Awerengedwenso

Anthu otsatira chipani cha Democrat mdziko la America ati akufuna kuti mavoti a chisankho chomwe chachitika  posachedwapa mdzikolo awerengedwenso. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC anthuwa anena...

View Article

Alamulidwa Kukakhala ku Ndende Zaka Zitatu Kamba Kogona Ndi Mnyamata Wopempempha

Bwalo loyamba la milandu m’boma la Machinga lalamula mzimayi wina wa zaka 26 zakubadwa kuti akakhale kundende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka zitatu kaamba kopezeka olakwa pa mlandu...

View Article

Papa Akuyembekezeka Kuyendera Dziko la Bangladesh

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko watumiza uthenga wa mafuno abwino komanso madalitso kwa anthu a mdziko la Bangladesh pamene akuyembekezeka kukayendera dzikolo masiku...

View Article

Mnangagwa Akuyembekezeka Kukhala Mtsogoleri wa Zimbabwe

Yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko la Zimbabwe a Emmerson Mnangagwa akuyembekezeka kulumbilitsidwa kukhala mtsogoleri wa dzikolo posachedwapa kutsatira kutula pansi udindo kwa yemwe anali...

View Article


Akaseweza Zaka 8 Kaamba Kogwililira Msungwana Wozelezeka

Bwalo loyamba la milandu m’boma la Ntchisi lalamula bambo wina wa zaka 46 zakubadwa kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka zisanu ndi zitatu (8) litamupeza olakwa pa...

View Article

ECM Ipempha Akhristu Atenge Mbali Pa Ulendo Wa Ndawala

Mpingo wa katolika mdziko muno molumikizana ndi mpingo wa evangelical wapempha akhristu onse mdziko muno kuti atenge nawo mbali pa ulendo wa ndawala womwe wakonzedwa kuti uchitike pa 6 mwezi wa mawa....

View Article


Mnangagwa Alonjeza Ufulu wa Chibadwidwe ku Zimbabwe

Yemwe akuyembekezeka kukhala mtsogoleri wa dziko la Zimbabwe a Emmerson Mnangagwa wati akufuna kuti dzikolo likhale latsopano lomwe anthu ake akhale ndi ufulu wawo wachibadwidwe. Malinga ndi malipoti...

View Article

Akhristu, Asilamu Akhale Omvetsetsana

Mchitidwe wosalana kaamba ka kusiyana pa zipembedzo ati ungathe mdziko muno ngati akhristu komanso asilamu akhala omvetsetsana mu zochita zawo. Mphunzitsi wa phunziro la chisilamu pa sukulu yosulira...

View Article


Anthu Aleke Kuchitirana Nkhanza

Anthu mdziko muno awapempha kuti aleke kuchitirana nkhanza wina ndi mzake komanso makamaka m’mabanja. Mkulu wa apolisi mchigawo cha kum’mawa kwa dziko lino, Commissioner Martha Suwedi ndi yemwe wanena...

View Article

Banki ya Reserve Iyamikira Banki Yaikulu pa Dziko Lonse

Banki yaikulu m’dziko muno ya Reserve yayamikira banki yaikulu padziko lonse ya World Bank kaamba ka thandizo lachuma lomwe limapereka pa chitukuko cha dziko muno. Mkulu wa banki-yi m’dziko muno a...

View Article

Reserve Banki Ilimbikitsa Anthu Kugwiritsa Ntchito Njira za Makono Zosungira...

Banki yayikulu m’dziko muno yaReserveyalimbikitsa anthu mdziko muno kuti azigwilitsa ntchito njira za makono zosungira ndi kutengera ndalama zomwe zikupelekedwa ndi ma bank komanso makampani ena...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>