Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Makwaya Akuyenera Kutsata Chiphunzitso cha Mpingo pa Kayimbidwe

$
0
0

Magulu oyimba mu mpingo wa katolika ati akuyenera kumayimba nyimbo zawo potsatira chiphunzitso cha mpingowu.

Mlangizi woyang’anira za chipembedzo komanso magulu oyimba mu Archdayosizi ya Blantyre Bambo Lazarus Zulani ndi omwe anena izi loweruka pa chikondwelero cha mayimbidwe chomwe makwaya a mu Dinale ya Limbe anakonza  mu Archdayosiziyo.

Bambo Zulani ati mpofunika kuti makwaya azilumikizana pafupifupi ndi atsogoleri awo pofuna kuti zomwe iwo akuyimba zizigwirizana ndi chiphunzitso cha mpingo.

Iwo ati ngati Bambo mlangizi wa Dinaleyo akufuna kuwonetsetsa kuti makwaya akutsata dongosolo loyenera pa kayimbidwe maka pa nkhani ya chipembedzo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>