Amayi a Mpingo wa Katolika Apemphedwa Kukwaniritsa Zomwe Akambirana Kumsonkhano
Episkopi wa dayosizi ya Mangochi Ambuye Montfort Sitima,wapempha mamembala a bungwe la amayi mu mpingowu kuti akwaniritse mfundo zomwe amanga kumsonkhano wawo waukulu, womwe watha lamulungu ku sukulu...
View ArticleMafumu a M’boma la Ntcheu Ayamikira Bungwe la CCJP
Mafumu m’boma la Ntcheu ayamikira ntchito yokhudza Chilungamo Choyambilira yomwe nthambi yowona za Chilungamo ndi Mtendere mu mpingo wakatolika mu arkidayosizi ya Lilongwe, imagwira m’bomalo ndi...
View ArticleAnthu 26 Afa ndi Mabomba M’dziko la Nigeria
Anthu 26 afa mabomba ataphulika mchigawo cha kumpoto kwa dziko la Nigeria. Mwa anthuwo,anthu makumi awiri,amwalira pa malo ena okwelera basi mtauni ya Gombe ndipo ena asanu ndi mmodzi amwalira ndi...
View ArticleBungwe la NAC Lakana Kulandira Ndalama Kuchokera kwa Anthu Khumi Amalonda
Bungwe lolimbana ndi matenda a Edzi mdziko muno la National Aids Commission NAC,lakana kulandira ndalama zokwana 5 miliyoni kwacha zomwe anthu ena amalonda anakabweza ku bungwelo mmalo mwa bungwe la...
View ArticleMabungwe Atengepo Mbali pa Ntchito za Ulimi
Ulimi mdziko muno ati ungathe kupita patsogolo mabungwe kuphatikizapo omwe siaboma, atatengapo mbali yaikulu pantchito za ulimi. Mmodzi mwa akuluakulu owona zaulimi mu nthambi ya zaulimi ya Chivala EPA...
View ArticleMsikana wa Zaka 13 Wagwidwa ndi Apolisi Mziko la Nigeria Pomuganizira Kuti...
M’sungwana wina wa zaka 13 akuti ali m’manja mwa apolisi mdziko la NIGERIA atamupeza kuti anali m’modzi mwa atsikana amene akhala akugwilitsidwa ntchito ndi zigawenga za gulu la Boko Haram kuti...
View ArticleAmbuye Ziyaye Afunila Akhirisitu Ampingo wa Katolika Mafuno Abwino A Khirisimasi
Episcope wa Arch-Diocese ya Lilongwe Ambuye Tarcizio Ziyaye afunila mafuno abwino akhilisimasi kwa akhristu onse ampingowu m’dziko muno. Ambuye Ziyaye anena izi dzulo utangotha mwambo wa nsembe yamisa...
View ArticleZigawenga Zipha Anthu Oposa Makumi Asanu ndi Limodzi Mdziko la India
Anthu oposera makumi asanu ndi limodzi afa pakumenyana komwe kwakhala kukuchitika pakati pa mitundu ina m’dziko la India. Nkulu wa apolisi a dzikoli wauza atolankhani m’dzikomo kuti limodzi mwa magulu...
View ArticleAnthu Atatu Afa Phanga Litawagumukila Ku Salima
Anthu atatu afa phanga lomwe amakumbamo miyala ya mtengo wapatali ya Garnet litawagumukira m’boma la Salima. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Gift Chitowe wati izi zachitika lachinayi pa...
View ArticleAsilikali Atatu a Bungwe la African Union Aphedwa Mdziko la Somalia
Asilikali atatu a bungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa la African Union ,aphedwa ndi zigawenga za gulu la Al-shaab kulikulu la bungweli mumzinda wa Mogadishu mdiko la Somalia. Malinga ndi lipoti...
View ArticleNtchito za Kusamalira a Mndende Zayenda Bwino mu Chaka cha 2014
Nthambi yoyang’anira chisamaliro cha anthu ku ndende mu ark-dayosizi ya Blantyre yati ndiyokhutira ndi momwe ntchito zake zayendera mchaka cha 2014. Bambo mlangizi oyang’anira nthambiyi mu...
View ArticleBoma Lili ndi Udindo Wosamalira Mabanja
Arkdayosizi ya Blantyre yati boma liri ndi udindo waukulu woonetsetsa kuti mabanja ovomerezeka mdziko muno, akusamalidwa moyenera. Ark-episikopi wa ark-dayosiziyi wolemekezeka Ambuye Thomas Luke Msusa...
View ArticleEpiskopi wa Archdayosizi ya Lilongwe Wadzudzula Mchitidwe wa Maukwati...
Episkopi wa Arch-diocese ya Lilongwe olemekezeka ambuye Tarcizio Ziyaye wati mchitidwe umene mayiko olemera akumachita polimbikitsa maukwati a pakati pa amuna kapena akazi okhaokha ndi amene...
View ArticleBungwe la MUB Lapindula ndi Ntchito Zake Mu Chaka cha 2014
Chaka cha 2014 akuti chidzakhala chaka chosayiwalika mu mbiri ya bungwe lomenyera ufulu wa anthu osaona la Malawi Union for The Blind (MUB). Mkulu wa bungwelia Ezekiel Kumwenda awuza Radio Maria Malawi...
View ArticleChiwerengero cha Atumiki Ophedwa a Mpingo Wakatolika Chakwera Mdziko la Mexico
Chiwerengero cha ansembe ndi atumiki ena a mpingo wa katolika omwe akhala akuphedwa akuti chakwera kwambiri mdziko la Mexico. Malinga ndi zotsatira za kafukufuku amene bungwe la Catholic Multimedia...
View ArticleMabungwe Olimbikitsa Ufulu Sakugwirizana ndi Ganizo la Ziwonetsero
Mabungwe ena olimbikitsa ufulu wa anthu mchigawo cha kummwera mdziko muno,ati sakugwirizana ndi ziwonetsero zomwe mabungwe ena omenyera ufulu wa anthu akukonza pa 13 mwezi uno wa January. Mkulu...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Yati Ana Akuyenera Kuyikidwa Patsogolo mu Nkhani Za Mpingo
Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi Ambuye Montfort Sitima ati ana akuyenera kuyikidwa patsogolo pankhani zokhudza mpingo. Ambuye Sitima alankhula izi lachitatu pa msonkhano wa mabungwe a ana otumikira...
View ArticlePapa Francisco Wapempha Akhristu kuti Akhale Okonda Kuchita Ntchito za Chifundo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu, kuti aziwonetsa chikhulupiliro chawo, pothandiza anthu ovutika komanso odwala matenda osiyanasiyana. Papa Francisco,...
View ArticleAmbuye Stima at Akhristu Akuyenera Kulemekeza Tsiku la Utumiki wa Ana
Episkopi wa Diocese ya Mangochi Ambuye Montfort Stima,ati akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno akuyenera kulemekeza tsiku la chaka cha Epifania , lomwe mpingo wakatolika unaliyika mwapadera kuti...
View ArticleMakwaya Akuyenera Kutsata Chiphunzitso cha Mpingo pa Kayimbidwe
Magulu oyimba mu mpingo wa katolika ati akuyenera kumayimba nyimbo zawo potsatira chiphunzitso cha mpingowu. Mlangizi woyang’anira za chipembedzo komanso magulu oyimba mu Archdayosizi ya Blantyre Bambo...
View Article