M’tsogoleri wa dziko la America a BarackObama ndi amene adzatsekere zokambirana ku msonkhano wa bungwe la zaumoyo la CatholicHeailthOrganisation umene ukuchitikira mu mzinda wa Washingtionm’dziko la America.
Akuluakulu a bungweli ndi amene alengeza izi ndipo ati mwambo wotsekera zokambirana za bungweli ku msonkhanowu udzachitika pa 9June2015.
Mwa zina nthumwi ku msonkhanowu, zikukambirana mfundo zikuluzikulu zothandizira kupititsa patsogolo ntchito za umoyo pa dziko lonse.