PULEZIDENTI BANDA WAKHUTIRA NDI MMENE MALONDA A FODYA AYAMBIRA
Pulezidenti Dr Joyce Banda wati ndi okondwa ndi mitengo yomwe alimi anagulitsira fodya wawo lolemba pamene amatsekulira msika wambewuyi chaka chino ponena kuti akukhulupirira kuti chaka cha 2014...
View ArticleMABUNGWE AKWIYA NDI KUYIMITSIDWA KWA NTCHITO YOWUNIKA MAYINA MKAWUNDULA
Anthu komanso mabungwe omwe sia boma ati sakugwirizana ndi zomwe bungwe la za chisankho la MEC lachita poyimitsa ntchito ya mugawo loyamba lowunika mayina mukawundula wa voti yomwe inayamba lolemba...
View ArticleA PAYONIYA AKUFUNA CHILUNGAMO KUCHOKERA KU BOMA
Mamembala a gulu lakale la boma la Malawi Young Pioneers [MYP] lachiwiri anakatula chikalata kwa pulezidenti Joyce Banda kudzera ku ofesi ya bwanamkubwa wa mboma la Lilongwe chopempha kuti alowererepo...
View ArticleDziko la Ethiopia ndi Lokonzeka Kuchititsa Msonkhano wa Amecea
Maepiskopi a m’dziko la Ethiopia ndi amene adzatsogolere msonkhano wa nambala 19 wa m’bungwe la Amecea . Msonkhanowu ndi wolingana ndi umene unachitikira m’dziko muno. Malingana ndi malipoti...
View ArticleMpingo wa Katolika Mdziko la Nigeria Waletsa Amayi Kuchotsa Pathupi
Mpingo wakatolika mdziko la Nigeria wati siwukugwirizana ndi ganizo loti amayi omwe adapatsidwa pathupi ndi mamembala a gulu la zigawenga za Boko Haram atagwidwa ukapolo,achotsedwe pathupipo. Mkulu...
View ArticleDziko la Burundi Liyimitse Chisankho
Atsogoleri a m’mayiko a mu Africa apempha boma la Burundi kuti liyambe layimitsa chisankho cha Pulezidenti chomwe lakonza kuti chichitike mwezi uno. Mipingo ndi mabungwe akhalanso akunena chimodzimodzi...
View ArticleBungwe la Aphuzitsi achi Katolika aliyamikila Popeleka Zachifundo
Bungwe la Aphunzitsi a Mpingo wa Katolika ozungulira Parish ya Mayaka mu Dayosizi ya Zomba aliyamikira kamba kozipereka pa ntchito zachifundo. Wothandizira Bambo Mfumu a pa Parishiyi Bambo James...
View ArticleAkhristu 49 akuno ku Malawi ankhala nawo pa Mwambo wa Misa Wokumbukila...
Akhristu 49 a mpingo wakatolika akuno ku Malawi, lachitatu anakhala nawo pamwambo wamapemphero okumbukira a maritiri 22 ku Namugongo Shrine mdziko la Uganda. Mmodzi mwa amaritiriwa Charles Lwanga Oyera...
View ArticleChiwelengelo cha Akhristu Achikatolika Chikukula
Lipoti lomwe nthambi yowona zakafukufuku pa sukulu ina ya ukachenjede mdziko la America yatulutsa lati chiwerengero cha akhristu a mpingo wakatolika padziko lonse chikukwera kwambiri maka mmaiko a mu...
View ArticleCadecom Inkhazikitsa Tchito Yonthandiza Anthu Mboma la Chikhwawa.
Dayosizi ya mpingo wakatolika ya Chikhwawa yati iwonetsetsa kuti ntchito za Bungwe lowona zachitukuko mumpingowu la CADECOM zikupindulira anthu onse mu Dayosiziyo. Episikopi wa Dayosiziyi wolemekezeka...
View ArticlePulesideti Balack Obama Adzatsekela Msonkhano Wa Bungwe la za Umoyo
M’tsogoleri wa dziko la America a BarackObama ndi amene adzatsekere zokambirana ku msonkhano wa bungwe la zaumoyo la CatholicHeailthOrganisation umene ukuchitikira mu mzinda wa Washingtionm’dziko la...
View ArticleKusintha Kwa Nyengo Kungachepe Ngati Boma Litasitsa Mitengo Yogulila Simenti.
Wapampando wakomiti yowona zachilengedwe ku nyumba ya malamulo wolemekezeka a Werani Chilenga anafokozela atolankhani kuti Vuto lakusintha kwa nyengo m’dziko muno lingachepe ngati boma litayesa njila...
View ArticleMavolotiya aku Radio Maria Awalangiza Kusogoza Mulungu Pamene Akutumikira ku...
Ma Volontiya wotumikila ku Mangochi Studiyo ya Radio Maria awalangiza kuti adzitsongoza Mulungu pamene akugwila tchito yotumikila kufalitsa uthenga wa Mulungu kudzela pa wailesiyi. Bambo Elizeo...
View ArticlePulesidenti Putin Akambilana ndi Papa Zonkhudza Mavuto Omwe Akuchitika ku...
Mtsogoleri wa dziko la Russia Pulesidenti Putin wachita zokambilana zake ndi mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ku likulu la mpingowu ku Vatican. Malingana ndi mkulu wa...
View ArticleBungwe La CCJP Lankhazikitsa Ntchito yolimbikitsa Maphuziro
Mfumu yayikulu m’boma la Mangochi a Sultan Chowe yayamikira bungwe la Chilungamo ndi Mtendele mu mpingo wa katolika la CCJP kamba kokhadzikitsa ntchito yomwe mwa zina ikulimbikitsa za maphunziro...
View ArticleAkhristu ochokela ku Lilongwe Arch-Diocese apempha akhristu mdziko muno...
Gulu lomwe lili paulendo wopita ku Yerusalemu lochokela mu Arch-Diocese ya Lilongwe lapempha Akhristu m`dziko muno kuti akuyenera kumatenga nawo gawo pamaulendo osiyanasiyana makamaka okapemphera...
View ArticleApolice Amanga Anthu Asanu Ogwila Ntchito pa Sitolo ya Chipiku.
Apolisi mboma la Neno amanga anthu asanu powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kubedwa kwa ndalama zoposela 4 Million mu sitolo ya chipiku m’bomalo. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, a...
View ArticleBoma la Malawi Ndilokonzeka Patchito Yotukula Mamphuziro a Atsikana.
President wa dziko lino Professor Peter Mutharika wati boma lake ndi lodzipereka pantchito yotukura maphunziro aatsikana. President Mutharika adayankhula zimenezi pamsonkhano omwe unakonzedwa ndi...
View ArticleBungwe la MEC Lakodzeka Kuchitisa Chisankho Mmadela Womwe Mulibe ma Nkhasala.
Bungwe lowona za Zisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission lati tsopano ndi lokonzeka kudzachititsa chisankho chachibwereza m`madela momwe mulibe makhansala m`dziko muno. Mmodzi mwa...
View ArticleAlimbikitsa akhritsu kupemphelela wansembe yemwe anabedwa ndizigawenga dziko...
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko la Nigeria awalimbikitsa kuti apemphelere wa nsembe wa mpingo wakatolika amene anagwidwa ndi anthu ena osadziwika m’dzikomo pa 8 mwezi uno. Wansembeyo yemwe...
View Article