Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

"IKANI MAPEMPHERO PATSOGOLO MU NYENGO YA PA PASAKA"-PRESIDENT JOYCE BANDA

$
0
0

 

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Joyce Banda wapempha akhristu kuti akondwelere kuwuka kwa Yesu khristu poika mapemphero patsogolo mu chikondwelero cha Pasaka.

President Joyce Banda walangizanso anthu omwe akukasangalala kutali ndi nyumba zawo kuti awonetsetse kuti  katundu wawo ali otetezedwa.

 Malinga ndi chikalata chomwe Ofesi yofalitsa nkhani ku nyumba ya boma yatulutsa, mtsogoleri wadziko linoyu walangizanso oyendetsa galimoto m'dziko muno kuti ayendetse galimoto mosamala mu  nyengoyi  popewa ngozi.

 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>