TIGWILANE MANJA POTHETSA UMBAVA-MASAUKO MEDI
Apolisi owona za chitetezo ku likulu la apolisi mu mzinda wa Lilongwe ati ayesetsa kugwira ntchito modzipereka ndi anthu a m’midzi pofuna kuthetsa m’chitidwe wa umbava ndi umbanda. Mkulu wa apolisi...
View ArticleAMBUYE STE MARIE APEMPHA AKHRISTU KUTI AZAMITSE CHIKHULUPILIRO
Arkiepiskopi wa Arkidayosizi ya Lilongwe ya Mpingo wa Katolika Ambuye Remi Ste Marie apempha akhristu a Mpingowu mu arkidayosiziyo kuti alimbitse chikhulupiliro chawo pomwenso akhristu a Mpingowu pa...
View ArticleBUNGWE LA MEC LAYIMITSA GANIZO LOGWILITSA NTCHITO MAKINA ATSOPANO PA CHISANKHO
Bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lati layimitsa ganizo lake lofuna kugwiritsa ntchito makina atsopano pa kalembera wa voti pokonzekera chisankho cha...
View ArticleWAYILESI ZA MARIA ZIKUFUNA KUTHANDIZA KUTI MAWAYILESI ENA AKHAZIKITSIDWENSO...
Wailesi za Maria zomwe zidakhazikitsidwa kale pa dziko la pansi zakonza dongosolo lofuna kuthandiza kukhazikitsa wayilesi zina m’mayiko momwe akufuna kukhalanso ndi wayilesi za amayi Maria pa...
View ArticlePAPA FRANCIS ACHEZA NDI MTSOGOLERI WOPUMA PAPA BENEDIKITO WA 16
Mtsogoleri wa Mpingo wa Katolika padziko lonse Papa Francis anakayendera ndikudya nkhomaliro ndi mtsogoleri opuma wa Mpingowu Papa Benedikito wa 16 loweruka pa 23 March 2013. Papa Francis...
View Article"IKANI MAPEMPHERO PATSOGOLO MU NYENGO YA PA PASAKA"-PRESIDENT JOYCE BANDA
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Joyce Banda wapempha akhristu kuti akondwelere kuwuka kwa Yesu khristu poika mapemphero patsogolo mu chikondwelero cha Pasaka. President Joyce Banda walangizanso anthu...
View ArticleBAMBO STEVEN SAULOSI MKATA ALOWA M'MANDA PA 2 APRIL 2013
Bambo Steven Saulosi Mkata omwe amwalira pa 30 March 2013 akuyembekezeka kuikidwa m’manda mwa ulemu lachiwiri likudzali pa 2 April 2013. Monsignor Mkata adamwalira ku pachipatala cha St Joseph ku...
View ArticleNDUNA IYAMIKIRA MGWIRIZANO PAKATI PA MIPINGO YA MU MZINDA WA MZUZU
Nduna ya za malimidwe ndi kuonetsetsa kuti m'dziko muno muli chakudya chokwanira Wolemekezeka a Peter Mwanza ayamikira mgwilizano wabwino omwe ulipo pakati pa Mipingo yozungulira mzinda wa Mzuzu. A...
View ArticleBOMA LIDZIPEREKA MALIPIRO ABWINO KWA OGWIRA NTCHITOZA CHIPATALA-DAVID KANKWAMBA
Mkulu wa bungwe la atolankhani omwe anapezeka ndi Kachilombo ka HIV komwe kamayambitsa matenda a Edzi la Journalists living with HIV and AIDS a David Kamkwamba apempha boma kuti lithandize pa nkhani...
View ArticleAPOLISI AGWIRA MWAMUNA OPEZEKA NDI MFUTI POPANDA CHILOLEZO
A polisi ku Mzuzu agwira ndi kutsekera m'chitolokosi mwamuna wina yemwe amasunga mfuti ziwiri za mtundu wa Green nala m’boma la Karonga . Mneneri wa a Polisi ku Mzuzu Sergeant Morris Chapola wati...
View ArticleCHIPANI CHA AFORD CHAKANA KUGWIRA NTCHITO CHIPANI CHOLAMULA
Mmodzi wa akuluakulu a chipani cha Alliance For Democracy (AFORD) watsutsa zomwe wayankhula wapampando wachipanichi a Enock Chakufwa Chihana kuti chipani cha AFORD chigwira ntchito ndi cha...
View ArticleKODI CHIZINDIKIRO CHANU NCHANI?
Ulaliki titled Kodi Chizindikiro Chanu Nchani? by Mayi Marita Senia Kaunda.
View Article