Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mneneri wa Chipani Chotsutsa cha UPD Mdziko la Burundi Waphedwa

$
0
0

Mneneri wa chipani china chotsutsa mdziko la Burundi waphedwa lolemba usiku atawomberedwa ndi anthu osadziwika mu mzinda wa Bujumbura.

Mneneriyu Patrice Gahungu anali wa chipani cha Union for Peace and Development UPD chomwe chinali chimodzi mwa zipani zotsutsa kuti pulezidenti wa dzikolo Pierre Nkurunziza asayimenso kachitatu pa udindowo.

Boma la dzikolo ladzudzula zipani zotsutsa kuti ndi zomwe zikuchititsa kuti ziwembu zipitilire kuchitika mdzikolo kaamba koti sizikugwirizanabe ndi utsogoleri wa pulezidenti Nkuruzinza.

Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu pafupifupi zana limodzi anaphedwa mdzikolo pa zipolowe zomwe zimachitika pulezidenti Nkuruzinza atalengeza kuti ayimanso kachitatu.

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>