Dziko la Swaziland Likufunika Mwambo wa Mapemphero
Episkopi wa dziko la Swaziland wapempha anthu m’dzikolo kuti akhale ndi mwambo wa mapemphero potsatira ngozi ya pansewu yomwe inapha atsikana pafupifupi makumi asanu omwe adali paulendo...
View ArticlePapa Francisco Wapepesa Anthu omwe Akhudzidwa ndi Mphepo ya Mkuntho
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco watumiza uthenga wa chipepeso kwa abale a anthu omwe akhudzidwa ndi mphepo ya mkuntho yomwe yachitika pa doko la Caribean . Mu uthengawo...
View ArticleBungwe la Mabanja Likondwelera Zaka 30 Chilikhazikitsire
Bungwe la mabanja mumpingo wa katolika m`dziko muno ati lichita chaka chokondwerela kuti latha zaka makumi atatu chilikhazikitsire m`dziko muno. Banja lomwe likutsogolera bungweli a Godfrey ndi a...
View ArticleMatupi a Asilikali Khumi a Mdziko la Uganda Apita Nawo Kwawo
Matupi khumi a asilikali a dziko la Uganda omwe anafa, gulu la zauchifwamba la Al-shabab litachita zamtopola kumalo omwe asilikaliwa amakhaka omwe ali pamtunda wamakilomita 90 kumm’wera chakunzambwe...
View ArticlePulezidenti wa Dziko la Guatemala Watula Pansi Udindo
Mtsogoleri wa dziko la Guatemala a Perezi Molina watula pansi udindo wake komanso amangidwa kamba komuganizira kuti amachita zakatangale. Malinga ndi malipoti a wailesi ya Vatican Pulezidenti...
View ArticleChipani cha SBVM Chikondwelera Zaka 90 Chikhazikitsire
Asisteri a Chipani cha atumiki a maria virgo woyera Sisters of the Blessed Virgin Mary SBVM mu mpingo wakatolika awayamikira kamba ka ntchito zosiyanasiyana zomwe akhala akugwia m’dziko muno....
View ArticleMatupi a Anthu 61 omwe Anafa pa Ngozi ya Bwato Mdziko la Malaysia Apezeka
Matupi a anthu 61 a mdziko la Indonesia omwe anafa pa ngozi ya bwato lomwe anakwera litamila lachinayi sabata yatha mdziko la Malaysia, apezeka lolemba. Malinga ndi malipoti a nyuzi 24 anthuwo...
View ArticleBungwe la AU Liwonetsetsa kuti Zisankho Mmayiko amu Africa Zikuyenda Bwino
Bungwe la African Union (AU) lati lili ndi udindo woonetsetsa kuti mabungwe oyendetsa zisankho m`mayiko a mu Africa ali ndi kuthekera koyendetsa zisankho mwabata ndi mtendere. M`modzi mwa akuluakulu...
View ArticleDziko la Guatemala Lichita Chisankho cha Pulezidenti
Anthu a mdziko la Guatemala achita chisankho chosankha mtsogoleri wina wa dzikolo. Chisakhochi chachitika mtsogoleri wa dzikolo a Perez Molina atatula pansi udindo wake komanso wamangidwa kamba koti...
View ArticleMneneri wa Chipani Chotsutsa cha UPD Mdziko la Burundi Waphedwa
Mneneri wa chipani china chotsutsa mdziko la Burundi waphedwa lolemba usiku atawomberedwa ndi anthu osadziwika mu mzinda wa Bujumbura. Mneneriyu Patrice Gahungu anali wa chipani cha Union for Peace...
View ArticlePapa Benedict wa 16 ndi Wokhudzidwa ndi Mavuto omwe Anthu Othawa Kwawo...
Mtsogoleri wampingo wakatolika wopuma Papa Benedict wa 16 ati ndi okhudzidwa ndi mavuto omwe anthu othawa kwawo chifukwa cha nkhondo komanso anthu omwe amachoka m`mayiko mwawo kamba kosowa ntchito,...
View ArticleChiwelengero cha Imfa za Ana Osakwana Zaka Zisanu Chatsika
Nthambi ya bungwe la United Nations lowona za Umoyo la World Health Organisation WHO lati chiwerengero cha imfa za ana osakwana zaka zisanu chatsika ndi mapereseti pafupifupi makumi asanu kuyambira...
View ArticleBungwe la CFM lakonza Msonkhano Wapachaka
Bungwe la mabanja a chikhristu mu mpingo wakatolika la Christian Family Movement CFM lati lidzipereka kukonza mfundo zothandiza kupititsa moyo wa m’banja patsogolo. Mkulu wa bungweli m’chigawo cha...
View ArticleChikondwelero cha Radio Maria Choir Festival Chikhala Chopambana
Chikondwelero cha mayimbidwe cha Radio Maria Malawi ati chikhala chopambana kusiyana ndi momwe zinthu zakhala zikuyendera mmbuyomu. Wapampando wa komiti yoyendetsa chikondwelero cha mayimbidwe a...
View ArticleMabanja Abwino Angabweretse Chitukuko mu Mpingo ndi Mdziko
Mpingo wakatolika mdziko muno wati umazindikira kuti kukhala ndi mabanja abwino kungathandize chitukuko cha mpingo komanso dziko. Episkopi wa dayosizi ya Chikwawa Ambuye Peter Musikuwa ndi omwe...
View ArticleBambo Nsope Apempha Ophunzira a Sukulu ya Ukachenjede ya Chancellor Kukhala...
Ophunzira achikatolika ku Chancellor College mu mzinda wa Zomba awapempha kuti azikonda kulimbikitsa makhalidwe abwino ndi okonda kupemphera nthawi zonse. Bambo Alfred Nsope ndi amene apereka...
View ArticlePapa Francisco ndi Okhudzidwa ndi Mavuto omwe Anthu Othawa Kwao Akukumana Nawo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse la pansi Papa Francisco wati dziko lapansi likukumana ndi mavuto aakulu a anthu omwe akuthawa mmayiko awo kamba ka nkhondo,njala komanso kusowa kwa...
View ArticleApolisi Mdziko la Egypt Apha Anthu Khumi ndi Awiri
Apolisi mdziko la Egypt apha mwa ngozi anthu khumi ndi awiri kuphatikizapo nzika ya mdziko la Mexico yomwe imakayenda mdzikolo. Anthuwo amayenda mugalimoto zinayi zomwe zinalowa kumalo ena...
View ArticleMnyamata Wazaka 17 Waba Njinga Yamoto M’boma la Ntchisi
Apolisi m’boma la Ntchisi amanga mnyamata wina wa zaka 17 zakubadwa yemwe akumuganizira kuti waba njinga ya moto ya ndalama zosachepera 295 sauzande kwacha. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali...
View ArticlePapa Francisco Wapempha Akhristu kuti Akhale Okonda Kuchita Ntchito za Chifundo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu, kuti aziwonetsa chikhulupiliro chawo, pothandiza anthu ovutika komanso odwala matenda osiyanasiyana. Papa Francisco,...
View Article