Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Senegal

$
0
0

Mtsogoleri wadziko la SENEGAL, a MARCY SALI wati akufuna kuti achepetse telemu yake yokhalira paudindowu ndi zaka ziwiri.

Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, a muofesi ya president m`dzikolo ati president SALI wachita izi ndicholinga cholimbikitsa ufulu wa demokalase.  Izi zichititsa kuti chisankho cha president m`dzikolo chidzachitike  m`chaka cha 2017 , m`malo mwa m`chaka cha 2019. Zomwe wachita presidentiyu akuti zapeleka chitsanzo chabwino cha atsogoleri odziwa za ubwino wolemekeza malamulo ndi kulimbikitsa ufulu wa democrase. A SALI omwe ndi azaka 52 anasakhidwa kukhala paudindowu m`chaka cha 2012 atangonjetsa president yemwe amalamulira dzikolo a ABDOULAYE WADE.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>