Quantcast
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Thyolo

Mfumu Boidi ya m’dera la mfumu yaikulu Chimaliro m’boma la Thyolo yati silekelera zoti ana atsikana azikakamizidwa zolowa m’banja adakali achichepere.

Mfumuyi yanena izi pa mkumano omwe inachita ndi makolo pamodzi ndi atsikana onse amene analowa m’banja asanakwanitse zaka 18 zakubadwa. Iyo yati onse opezeka kuti akukolezera mchitidwewu adzayenera kulandira chilango popeleka chindapusa.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>