Mpingo wa Katolika Wafunira Akhristu Zabwino mu Nyengo ya Lenti
Mpingo wakatolika kuno ku Malawi wafunira akhristu komanso a malawi onse mafuno abwino,pamene lero ayamba ulendo wa masiku makumi anayi okumbukira masautso a Yesu Khristu. Polankhula ndi Radio Maria...
View ArticleDziko la America Lithana ndi Zigawenga
M’tsogoleri wa dziko la America a Barack Obama wati dziko la America liyesetsa pothana ndi magulu a zigawenga omwe akulimbikitsa ziwembu m’mayiko osiyanasiyana. Iye walakhula izi pokhudzidwa ndi...
View ArticleMakolo Alimbikitse Maphunziro
Mtsogoleli wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha makolo kuti adzipereke pa ntchito yokweza maphunziro pakati pa ana. Papa walankhula izi ku likulu la mpingowu ku Vatican pomwe...
View ArticlePapa Francisco Atsekulila Chaka cha Chifundo cha Mulungu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati pofuna kulowa pa khomo la nyumba ya atate akhristu akuyenera kuzindikira za chifundo chomwe Mulungu ali nacho pakati pa wina aliyense....
View ArticleBoma la Dziko la Egypt Alipempha kuti Lipereke Chitetezo ku Mipingo ya Mdzikolo
Mabungwe omenyala ufulu wa anthu mdziko la Egypt apempha boma la dzikolo kuti likhwimitse chitetezo ku mipingo ya mdzikolo. Ma bungwewa apereka pempheloli potsatira chiwopsezo chomwe mpingo wa...
View ArticleBungwe la SA Medicines Control Council Livomela Mankhwala Othandiza kupewa...
Bungwe la South Africa Medicines Control Council mdziko la South Africa lavomeleza kuti mankhwala omwe anapangidwa pofuna kupewa kutenga kwa kachilombo a HIV ayambe kugwira ntchito mdzikomo....
View ArticleChipani cha Mofolo Chidzoza a Blazala Awiri Kukhala Madikoni
A Blazala awiri a chipani cha Mofolo woyera loweruka awadzodza kukhala madikoni mu mpingo wakatolika . Mwambowu omwe unachitikira ku parish ya St Louis Montfort ku Balaka anatsogolera ndi episkopi...
View ArticlePapa Wati Maria Anawona Chifundo cha Mulungu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati Maria mai wa mpulumutsi anaona chifundo cha mulungu kamba koti anakhala ndi pakati pa mzimu woyera. Papa amalankhula izi loweruka ku...
View ArticleAnthu Pafupifupi 50 Afa Mdziko la BurundiAnthu Pafupifupi 50 Afa Mdziko la...
Anthu pafupifupi makumi asanu ndi anayi afa potsatira zipolowe zomwe zinachitika mmadera atatu okhala asilikali mdziko la Burundi. Malipoti a wayilesi ya BBC ati mwa anthu omwe aphedwawo matupi a...
View ArticleAna 1 Miliyoni a Mdziko la Nigeria ndi Mayiko Atatu Sakupita ku Sukulu
Malipoti a nthambi ya United Nations yoona za chisamaliro cha ana yapeza kuti chiwerengero cha ana 1 miliyoni a mdziko la Nigeria komanso maiko atatu oyandikana ndi dzikolo sakupita ku sukulu kaamba ka...
View ArticlePapa Francisco Akatsogolera Mwambo wa Misa wa Banja Loyera
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco akuyembekezeka kukatsogolera mwambo wa misa ya Banja loyera ku tchalitchi lalikulu la St Peter’s Basilica lamulungu likudzali mu mzinda wa...
View ArticleAnthu Othawa Kwawo 40 Afa
Anthu othawa kwao pafupifupi makumi anayi apezeka atafa pa nyanja ina boti lomwe anakwera litamira mdziko la Turkey. Malipoti a nyuzi 24 ati ngoziyo yomwe ndi kuphatikizapo ana yachitika pomwe anthuwa...
View ArticleBambo Zinyongo Amwalira
Bambo Rhodrick Zinyongo omwe amatumikira mu dayosizi ya mpingo wa katolika ya Dedza amwalira. Malinga ndi a ku likulu la mpingowu mu dayosiziyo, Bambo Zinyongo amwalira lachitatu mmawa. Bambo Zinyongo...
View ArticlePapa Abatiza Ana 26 pa Tsiku la Ubatizo wa Ambuye Yesu
Pomwe mpingo wa katolika umachita chaka cha ubatizo wa ambuye Yesu mumtsinje wa Yolodani , mtsogoleri wa mpingo wakatolika anabatiza makanda 26 ku Roma. Papa Francisco wabatiza anawa pa mwambo wa...
View ArticleMpingo wa Katolika Walimbikitsa za Kuthetsa Lamulo Lonyonga
Mpingo wa katolika ku Vatican wabwereza kupempha mayiko pa dziko lonse kuti athetse lamulo la kupha kwa anthu olakwira malamulo. Kazembe wa mpingowu ku bungwe la m’gwirizano wa maiko la United Nations...
View ArticlePapa Francisco ndi Wokhudzidwa ndi Mchitidwe Wogulitsa Mankhwala Ozunguza Bongo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndiwokhudzidwa ndi kuchuluka kwa anthu omwe amachita malonda ogulitsa mankhwala ozunguza bongo. Papa Francisco amalankhula izi...
View ArticleBungwe la Partners In Health lati lidzipereka pa Chisamaliro cha Amayi ndi Ana
Bungwe lothandiza anthu pa nkhani za umoyo ndi kadyedwe kabwino la Partners in Health lati lidzipereka powonetsetsa kuti amayi oyembekezera ndi ana akulandira chisamaliro chabwino pa miyoyo yawo....
View ArticleSenegal
Mtsogoleri wadziko la SENEGAL, a MARCY SALI wati akufuna kuti achepetse telemu yake yokhalira paudindowu ndi zaka ziwiri. Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, a muofesi ya president m`dzikolo ati...
View ArticleThyolo
Mfumu Boidi ya m’dera la mfumu yaikulu Chimaliro m’boma la Thyolo yati silekelera zoti ana atsikana azikakamizidwa zolowa m’banja adakali achichepere. Mfumuyi yanena izi pa mkumano omwe inachita ndi...
View ArticleUfa Ochokera Mdziko La Zambia Ukupulumutsa Miyoyo Ya Anthu Ambiri Mdzikomuno
Pamene Chimanga m’msika ya m’dziko muno chakwera kwambiri kuyerekeza ndi misika ya boma ya ardmark ufa ochokera mdziko la Zambia ndiomwe ukuthandiza kawmbiri anthu am’dziko muno. Ufa wochokera ku...
View Article