Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Papa wati Chifundo cha Mulungu Chimafafaniza MachimoPapa wati Chifundo cha Mulungu Chimafafaniza Mac

$
0
0

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati akhristu akuyenera kuzindikira kuti chifundo cha Mulungu chomwe alinacho pa wina aliyense, chimafafaniza machimo ngati momwe zovala zimayelera zikachapidwa.

Papa amalankhula izi ku likulu la mpingowu pa mapemphero omwe amakhala nawo lachitatu lililonse ndi anthu ochokera mmaiko osiyanasiyana pa bwalo la tchalitchi la St Peter’s mu mzinda wa Rome.

Papa anauza anthu omwe anasonkhanawo kuti ngati pali munthu wina yemwe sanachimwepo chikhalire akweze manja.

Iye wati akhristu akuyenera kupempha amayi Maria omwe ali a chifundo kuti awathandize pokhala okhululuka komanso kukhala ndi mtima watsopano.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>