Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Pulezidenti Zuma Sachotsedwa pa Udindo Wake

$
0
0

Nyumba ya malamulo m’dziko la South Africa inachita chisankho chakuti asachotse pa udindo mtsogoleri wa dzikolo a Jacob Zuma posayang’anira chigamulo chomwe bwalo lamilandu linapereka pa mlandu omwe limamuzenga.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC chipani cholamula mdzikolo cha African National Congress ANC Pulezidenti Zuma sanali olakwa pa mlanduwo ndipo nyumbayo itaponya voti yofuna kuchotsa mtsogoleriyu, chipanichi chinagonjetsa zipani zotsutsa kuti pulezidentiyo sakuyenera kutula pansi udindo wake.

Zipani zotsutsa boma mdzikolo zikufuna kuti pulezidenti Zuma atule pansi udindo wake ati kamba koti anagwiritsa ntchito ndalama za boma pokonzetsera nyumba yake yapadera.

Trending Articles

Mdima unadetsa dziko

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>