Chifundo cha Mulungu ndi cha Aliyense
Ark-episkopi wa mzinda wa Vienna mdziko la Australia Ambuye Christopher Schonborn wati chifundo cha Mulungu chilipo kwa aliyense amene amakhala akusawutsidwa mu mtima. Malinga ndi malipoti a wailesi...
View ArticleMunthu Mmodzi Wafa ndi Matenda a Ebola Mdziko la Liberia
Munthu m`modzi ati wafa ndi matenda a Ebola m`dziko la Liberia patangotha miyezi yowerengeka, bungwe la zaumoyo pa dziko lonse litalengeza kuti nthendayi yatha m`dzikolo. Malinga ndi malipoti...
View ArticleAmbuye Musikuwa Akhazikitsa Mijigo mu Dayosizi YawoAmbuye Musikuwa...
Mpingo wa katolika mu dayosizi ya Chikwawa wapempha boma ndi mabungwe akufuna kwabwino kuti alimbikitse ntchito yosamalira anthu omwe akuvutika kamba kosowa zinthu zofunika pamoyo wao wa tsiku ndi...
View ArticleDziko la Kenya Lichita Mapemphero a Ophunzira a pa Sukulu ya Garissa
Anthu m`dziko la Kenya achita mapemphero okumbukira mizimu ya anthu 148 omwe anafa pa chiwembu chomwe gulu la zigawenga za Al- Shabab zinachita pa sukulu ya ukachenjede ya Garisa m`dzikolo. Malinga...
View ArticleAbwenzi ndi Otumikira Radio Maria mu Dayosizi ya Zomba Alonjeza Kugwilira...
Ngati njira imodzi yopititsira patsogolo ntchito za Radio Maria Malawi, abwenzi a wailesiyi ku dayosizi ya Zomba ati agwira ntchito limodzi ndi otumikira a wailesiyi potolera thandizo. Wapampando wa...
View ArticlePapa Francisco wati Akhristu Akhale Apostoli komanso Wapempha Mtendere Mdziko...
Pamene mpingo umachita chaka cha lamulungu la chifundo, mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti akhale apostoli a chifundo kwa onse osowa. Malipoti a...
View ArticleMalema Ayimitsidwa ndi Apolisi pa Nseu
Apolisi m`dziko la South Africa ati anayimitsa galimoto la mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Economic Freedom Fighters (EFF) a Jullious Malema, potsatira zomwe mkuluyu ananena masiku apitawa...
View ArticleAmuna Atatu Amangidwa Chifukwa Cholima Chamba
Apolisi m’boma la Ntchisi akusunga mchitokosi amuna atatu kamba kowaganizira kuti amalima chamba. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergent Gladson M’bumpha watsimikiza za nkhaniyi. Sergent...
View ArticlePapa Wapempha Akhristu kuti Azivomera Kuyitana kwa Mulungu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti azikhala ndi mitima yotsekula kwa Mulungu nthawi zonse komanso azivomera kulandira uthenga wake wa chipulumutso....
View ArticlePulezidenti Zuma Sachotsedwa pa Udindo Wake
Nyumba ya malamulo m’dziko la South Africa inachita chisankho chakuti asachotse pa udindo mtsogoleri wa dzikolo a Jacob Zuma posayang’anira chigamulo chomwe bwalo lamilandu linapereka pa mlandu omwe...
View ArticleMpingo wa Orthdox Mdziko la Greece ndi Wokonzeka Kulandira Papa Francisco
Mpingo wa Orthodox mdziko la Greece wati ndi wokonzeka kulandira mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco paulendo wake wokayendera anthu othawa kwawo mdzikolo. Malipoti a wailesi...
View ArticleDziko la Egypt Litumiza Zotsatira za Kafukufuku wa Ophunzira yemwe Anaphedwa...
Dziko la Egypt lati litumiza zomwe lapeza pa kafukufuku wokhudza kuphedwa kwa ophunzira wa mdziko la Italy yemwe anapezeka atafa m`dziko la Egypt. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, ophunzirayo...
View ArticlePapa Francisco wati Akhristu a Mpingo wakatolika ndi Methodists Agwlire...
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati akhristu a mpingo wakatolika ndi Methodists akuyenera kuphunzirana kamba koti zolinga zawo ndi zimodzi. Papa Francisco amalankhula izi...
View ArticlePapa wati Mabanja Okhazikika Amakhala OpindulaPapa wati Mabanja Okhazikika...
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati mabanja okhazikika amakhala opindula kamba koti amachititsa kuti anthu azikhala bwino mmadera komanso ana amakula ndi chikondi,...
View ArticleMpingo Wakatolika ku Burundi Wapempha Mtsogoleri Wa Dzikolo Kuti...
Bungwe la ma Episkopi a mpingo wa Katolika m’dziko la Burundi lati silikugwirizana ndi zomwe m’tsogogoleri wa dzikolo akufuna kuti adzayimenso pa chisankho cha president kamba koti matelemu ake...
View ArticleRadio Maria Ikhazikitsidwa Mdziko la Madagascar
Akuluakulu oyendetsa ntchito za Radio Maria pa dziko lonse alengeza zakubadwa kwa wailesi ina m’dziko la Madagascar Kukhadzikitsidwa kwa wailesiyi kwachulukitsa nambala ya mayiko amene ali ndi Radio...
View ArticleAbwenzi a Radio Maria Malawi Awonetsa Chidwi pa Ntchito ya Mariatona
Akuluakulu a Radio Maria Malawi ayamikira abwenzi a wayilesiyi kamba kowonetsa chidwi chogwirira ntchito limodzi munyengo ino yomwe wailesiyi ikukonzekera ntchito ya chaka chino yotolera thandizo...
View ArticleMkhristu Wakufuna Kwabwino Apereka Malo ku Radio Maria
Mmodzi mwa akhristu mu mpingo wakatolika wapereka malo ku Radio Maria Malawi ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota ndi cholinga choti wailesiyi idzalepo transmitter yake. Mkhristuyu Martin Mangani wapereka...
View ArticleGuelleh Wapambananso pa Mpando wa PulezidentiGuelleh Wapambananso pa Mpando...
Mtsogoleri wa dziko la Djibouti a Ismail Omar Guelleh wapambananso pa chisankho chomwe chinachitika m`dzikolo masiku apitawa. Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, a Guelleh apeza mavoti 87 pa 1...
View ArticlePapa wati Mabanja Okhazikika Amakhala Opindula
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati mabanja okhazikika amakhala opindula kamba koti amachititsa kuti anthu azikhala bwino mmadera komanso ana amakula ndi chikondi,...
View Article