Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Kusowa kwa Chakudya

$
0
0
Boma lati laika ndondomeko zomwe ati zithandize pothana ndi vuto la chakudya lomwe lili m'dziko muno. Nduna ya zaulimi ,ulimi wa nthirila komanso chitukuko cha madzi Dr.Goerge Chaponda ndiwo anena izi poyakhula ndi atolankhani munzinda wa Lilongwe pomwe amapereka chinthunzithunzi chamomwe zithu ziliri m'dziko muno pankhani yachakudya komanso zomwe mboma likuchita pothana ndikusowa kwa chakudya komanso kuonetsetsa kuti vuto la njala litheretu m'dzikomuno. Dziko lino lalephera kukolora chakudya chokwanira kaamba kakusintha kwa nyengo komwe kwakhudza kwambiri ulimi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>