Achinyamata abungwe la YCW mu Doyisizi ya Mangochi awapempha kuti adzidzipeleka pomwe apasidwa kuti agwire ntchito m'malo osiyana siyana
Avicar General adoyosiziyi bambo Andrew Nkhata ndi omwe anena izi lamulungu lapitali pomwe achinyamata am'bungweri amachita mwambo wokondwelera nkhonswe yawo joseph wa ntchito padziko lonse mwambowu unachitikira ku St.Augustine Cathedral mu Doyosizi ya Mangochi.
↧