Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Mariatona

Mariatona ndi ndi dongosolo lapadela  limene limachitika  ndi cholinga chofuna kupeza ndalama, ndipo amene amakhudzidwa ndi onse woyendetsa  ntchito za wailesi  monga  ma volunteer, abwenzi a Radio...

View Article


Anthu Achitepo Kanthu Pofuna Kuchepetsa Imfa za pa Nyanja

Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha mayiko padziko lonse kuti achitepo kanthu pofuna kuchepetsa imfa za anthu omwe akumwalira panyanja, paulendo opita mmayiko a ku...

View Article


Bungwe la Law Society ndi lokhudzidwa ndi Mavuto omwe Dziko Lino Likukumana Nawo

Bungwe lowona za malamulo mdziko muno la Law  Society lati ndi lokhudzidwa kwambiri ndi mavuto omwe dziko lino layamba kukumana nawo posachedwapa pankhani zosiyanasiyana. Ena mwa mavuto omwe bungweli...

View Article

Msonkhano Wa Bungwe La Tilitonse Wachitika Ku Lilongwe

Msonkhano wa aphunzitsi a m’bungwe la utumiki wa ana la Tilitonse wachitika mu arkidayosizi ya mpingo wakatolika ya Lilongwe. Ofesi yoona za ma utumiki a Papa la Pontifical Missionary Societies (PMS)...

View Article

Boma Liyamikira Bungwe La St. Egidio Polimbikitsa Kaundula

Boma la Malawi layamikira mpingo wakatolika mdziko muno kamba kotengapo mbali pa ntchito yolimbikitsa anthu kuti azilembetsa ana awo mukaundula wa dziko lino, akabadwa. Mkulu woyendetsa ntchito yolemba...

View Article


Dayosizi Ya Zomba Ipempha Anthu Kuthana Ndi KunyentcheraDayosizi Ya Zomba...

Ofesi ya za umoyo mu dayosizi ya mpingo wakatolika ya Zomba yalimbikitsa anthu a mdera la Chingale kuti azidzipeleka polimbana ndi mavuto a kunyentchera pakati pa ana awo. Mlangizi wa sukulu za m’mera...

View Article

Bishop Elect for Mzuzu

KNOW THE BISHOP - ELECT FOR MZUZU DIOCESE ■HIS CURRICULUM VITAE ●Reverend Father John Alphonsus Ryan was born on 27 February, 1952 in Tipperary (Archdiocese of Cashel and Emily - Ireland) ●After his...

View Article

New Bishop Of Mzuzu Diocese

26thApril, 2016 His Excellency Archbishop Julio Murat, Apostolic Nuncio to Malawi and Zambia wish to announce that His Holiness Pope Francis has appointed Reverend Father John Alphonsus Ryan of the...

View Article


Episikopi Watsopano Wa Diyosizi Ya Mzuzu

Wolemekezeka Ambuye Julio Murat nthumwi ya a Papa m’maiko a Malawi ndi Zambia yalengeza kuti  mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko wasankha  Reverend Fr. John Alphonsus Ryan...

View Article


Machar Alumbilitsidwa Kukhala Wachiwiri kwa Pulezidenti

Mkulu wa gulu lowukira boma m’dziko la South Sudan Riek Machar amulumbiritsa kukhala wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dzikolo ndi cholinga chofuna kukometsa pangano lodzetsa mtendere ndi m’tsogoleri wa...

View Article

Papa Alimbikitsa Kufunika kwa Akhristu

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisco wauza ansembe kuti akuyenera kutumikira anthu nthawi zonse osati kuti azikhala patsogolo kupanga mfundo zoyendetsera mpingo kaamba koti...

View Article

Milandu ya Katengale ya Pulezidenti Zuma Iwunikidwenso

Bwalo lamilandu mdziko la South Africa lati ganizo lothetsa milandu 7 hundred 83 ya katangale ya pulezidenti wa dzikolo Jacob Zuma likuyenera kuwunikidwanso. Malipoti a wailesi ya BBC ati milanduyi...

View Article

Papa Alimbikitsa Anthu Kupereka Chisamaliro kwa Odwala

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati anthu akuyenera kukhala ndi chifundo ndi anthu omwe akudwala matenda osiyanasiya mmadera omwe amakhala. Papa amalankhula izi  ku...

View Article


Kusowa kwa Chakudya

Boma lati laika ndondomeko zomwe ati zithandize pothana ndi vuto la chakudya lomwe lili m'dziko muno. Nduna ya zaulimi ,ulimi wa nthirila komanso chitukuko cha madzi Dr.Goerge Chaponda ndiwo anena izi...

View Article

Bungwe la YCW mu Doyosizi Ya Mangochi

Achinyamata abungwe la YCW mu Doyisizi ya Mangochi awapempha kuti adzidzipeleka pomwe apasidwa kuti agwire ntchito m'malo osiyana siyana Avicar General adoyosiziyi bambo Andrew Nkhata ndi omwe anena...

View Article


Dayosizi Ya Zomba Yaphunzitsa Achinyamata Luso Losiyanasiyana Dayosizi Ya...

Achinyamata a kwa Mayaka m’boma la Zomba akuyimba lokoma ndi luso la ntchito zosiyanasiyana zomwe aphunzira kuchokera ku nthambi ya za maphunziro mu mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba....

View Article

ECM Yapempha Komiti Ya Ophunzira Msukulu Zachikatolika Zaukachenjende...

Komiti yatsopano ya bungwe la ophunzira achikatolika a msukulu za ukachenjede m’dziko muno   ayipempha kuti idzipeleke pa ntchito zotukula bungweli m’dziko muno. Mlangizi wa achinyamata ku likulu la...

View Article


ECM Lapereka ndalama ku Bungwe la MISA Malawi

Likulu la mpingo wa katolika dziko muno ECM,kudzera ku nthambi yake ya zachitukuko ya Social Development Directorate lapereka ndalama zokwana 5 hundred thousand kwacha ku bungwe la atolankhani la MISA...

View Article

Mwambo Wotsekulira Mariatona 2016

Mwambo wotsekulira Radio Maria Mariatona 2016 uchitika mawa ku Parish ya St.Louis Montfort ku Balaka mu dayosizi ya Mangochi,pali chikonzero choti akatsogolere misa yotsekulira Mariatona ndi ambuye...

View Article

Bungwe la Maneb Lapempha Magulu kuti Adzipereke

Bungwe lowona za mayeso mdziko muno la National Examinations Board MANEB,lapempha magulu osiyanasiyana kuti adzipereke powonetsetsa kuti vuto lobera mayeso lipitilire kuchepa mdziko muno. Mkulu owona...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>