Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Radio Maria Mariatona 2016

$
0
0
Radio Maria Malawi mogwirizana ndi Ma Radio ena onse pa dziko lonse la pansi Mawa akuyamba ulendo wa masiku atatu umene umatchedwa kuti Mariatona, kuno ku Malawi ulendowu unayamba loweruka pa 7 May ku Balaka parish Mu diocese ya Mangochi. Cholinga cha mariatona kuno ku Malawi ndi kupeza ndalama zokwana ten million kwacha zimene zigwire ntchito monga kumangira Goloto, kulipira License ku Macra ndi kugulira Back Up Power Sysstem.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>