Zuma wati Dziko Lake ndi la Mtendere
Mtsogoleri wa dziko la South Africa Jacub Zuma wati anthu amene amachitira alendo ziwembu mdzikolo ndi ochepa kwambiri poyerekeza ndi anthu omwe amakonda mtendere. Pulezidenti Zuma wanena izi lachisanu...
View ArticleRadio Maria Malawi Ipambana pa Nyimbo ya Mariatona
Radio Maria Malawi yapambana mu mpikisano wopeka ndi kujambula nyimbo yofalitsa uthenga wa Mariatona wa chaka chino mmawailesi a Radio Maria amu Africa. Nyimbo yomwe inapekedwa ndi kuyimbidwa ndi...
View ArticleNduna ya a Papa Yati Ndiyokhutira ndi Mpingo mu Dayosizi ya Mangochi
Nduna ya a papa m’mayiko Malawi ndi Zambia, Arch-Bishop Julio Murat yati ndi yokhutira ndi momwe chipembedzo cha mpingowu chikuyendera mu dayosizi yaMangochi. Ambuye Murat anena izi ku Mangochi...
View ArticleNduna ya a Papa ku mayiko a Malawi ndi Zambia Imemeza Anthu Kuthandiza Radio...
Nduna ya a Papa m’mayiko a Malawi ndi Zambia , Arch-Bishop Julio Murat walimbikitsa akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti atenge umwini wothandiza Radio Maria chifukwa ndi chida chodalilika mu...
View ArticlePapa Francisco Ayamikira Asilikali pa Ntchito Yabwino
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira asilikali omwe amagwira ntchito ya chitetezo ku likulu la mpingowu ku Vatican pa ntchito yabwino yomwe amagwira. Papa...
View ArticleBungwe la NYD likhazikitsa Pulojekiti ya Chisankho cha Moyo Wanga
Pofuna kuwonetsetsa kuti atsikana ndi amayi akulimbikitsidwa pa ntchito yodziyimira pawokha, bungwe lomwe si laboma la Network for Youth Development likhazikitsa ndondomeko ya ndalama zokwana 25...
View ArticleAmayi a MpingoWakatolika Alimbikitsa Ubale Pakati Pawo
Amayi mpingo wakatolika kwa Chikapa mu Parish ya Nthawira mu arki dayosizi ya Blantyre awayamikira kamba kolimbikitsa ubale wabwino pakati pawo ndi amayi a ku parish ya Chisitu ku Mulanje mu arki...
View ArticleAkhristu Awalimbikitsa Kupeleaka Masika
Akhristu alimana la St .Joseph ku St.John Church m'parish ya Kausi mu Diocese ya Mangochi awalimbikitsa za ubwino wopeleka mowolowa manja pa miyambo yonse yochitika mu mpingowu. Bambo mfumu a parishiyi...
View ArticleRadio Maria Mariatona 2016
Radio Maria Malawi mogwirizana ndi Ma Radio ena onse pa dziko lonse la pansi Mawa akuyamba ulendo wa masiku atatu umene umatchedwa kuti Mariatona, kuno ku Malawi ulendowu unayamba loweruka pa 7 May ku...
View ArticleMaprogramu Amariatona
Radio Maria Malawi lero lachisanu pa 13 May 2016 yayamba kuulutsa maprogramu amasiku atatu a Mariatona. Kudzera m'maprogramuwa anthu akumapeleka thandizo lawo ku wailesiyi ndipo pakufuni ndalama...
View ArticleTsiku Lachiwiri Ulendo Wa Mariatona .
Pamene mariatona akupitira Radio Maria ikupempha anthu onse amene amakonda wailesiyi kupitira kutenga nawo ku maprogram wosiyana siyanasiyana komanso kupereka ndalama kudzera ma pledge Card amene...
View ArticleAnthu Pafupifupi 6 Thousand Agwidwa pa Nyanja ya Mediterranean
Anthu oposa 5 sauzande 800,agwidwa mu nyanja ya Mediterranean sabata yapitayi, pamene anthu ogwira ntchito yowona zachitetezo cha anthu pa nyanjayo akhwimitsa chitetezo. Pantchitoyi achitetezowo, apeza...
View ArticleAnthu 137 Amila pa Nyanja ya Mediterranean
Malipoti akusonyeza kuti anthu 137 ndi omwe amwalira munyanja ya Mediterranean bwato lomwe anakwera litamira pa doko la Sicily mdziko la Italy. Malipoti a Wailesi ya BBC ati anthu makumi ndi anayi ndi...
View ArticleApolisi M’boma la Balaka Alangiza Woyendetsa Galimoto Kugwilitsa Tchito...
Apolisi m’boma la Balaka alangiza anthu oyendetsa galimoto kuti adzigwiritsa ntchito zizindikiro zapanseu pofuna kupewa ngozi. Apolisiwa apereka langizoli msungwana wazaka khumi ndi zitatu ndi bambo...
View ArticleTsiku Lachitatu La Mariatona
Radio Maria Malawi lero lamulungu ikhala ikupitllira kuwulutsa maprograme osiyana siyana apadela a mariatona uwu ndi ulendo wothamanga ndi a Mayi Maria kwa masiku atatu pofuna kupeza thandizo...
View ArticleArkidayosizi ya Blantyre
Arkiepiskopi wa arkidayosizi ya Blantyre ambuye Thomas Luke Msusa apempha akhristu a mu arkidayosiziyi kuti alimbikire kuthandiza mpingo kufalitsa uthenga wa Mulungu pamene mpingo ukukula. Arkiepiskopi...
View ArticleRadio Maria yatsekera Ulendo Wa Mariatona
Radio Maria dzuro lolemba yatsekera Ulendo wa masiku atatu wothamanga ndi Amayi Maria pa mapologalamu a padela a mariatona komabe ulendo wonse wotsekera mariatonayu udzakhalapo pa 2 July 2016 ku...
View ArticlePapa Fransisko Wati Mpingo Usasale Anthu Othawa Kwao
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse, Papa Fransisko, anachita zokambirana ndi atolankhani a nyuzipepala ina ya m’dziko la France komwe mwa zina wakambapo udindo wa mpingo m’maiko a ku Ulaya...
View ArticleMariatona Akupitilirabe
Ma pologalamu akathithi a Ulendo wa masiku atatu wothamanga ndi amayi Maria ndi cholinga chofuna kupeza thandizo loyendetsera Radio Maria atha lolemba. Koma malinga ndi akuluakulu a wailesiyi ati...
View ArticleNdege ina ya mdziko la Egypt Yasowa
Ndege ina ya mdziko la Egypt yomwe imachokera mu mzinda wa Paris kupita mu mzinda wa Cairo ati yasowa mu mlengalenga itanyamula anthu okwana 66. Malinga ndi malipoti ndegeyo ati yasowa kuzambwe kwa...
View Article