Radio Maria Malawi lero lamulungu ikhala ikupitllira kuwulutsa maprograme osiyana siyana apadela a mariatona uwu ndi ulendo wothamanga ndi a Mayi Maria kwa masiku atatu pofuna kupeza thandizo lothandizila ntchito za wailesiyi cholinga cha chaka chino ndi kupeza ndalama zokwana 10 million kwacha zimene ndi zomangira Goloto, kugulira Back up power System ndi kulipira ku Licenses ya Macra.
↧