Radio Maria dzuro lolemba yatsekera Ulendo wa masiku atatu wothamanga ndi Amayi Maria pa mapologalamu a padela a mariatona komabe ulendo wonse wotsekera mariatonayu udzakhalapo pa 2 July 2016 ku Chilomoni mu Arki dayosizi ya Blantyre . kuyambira mawa pazikhala mapologalamu ena a mariatona koma a patali patali.Radio Maria Malawi ikuthokonza onse amene atenga nawo mbari pa ma pologalamuwa mmasiku anayi.
↧