Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mpingo Udzudzula Boma Polanda Malo Kwa Anthu Akumidzi

$
0
0

Mpingo wa katolika m`dziko la Angolawa dzudzula m`chitidwe wa akuluakulu a boma omwe akumalanda malo anthu a kumidzi ndi ku ma kawapeleka kwa anthu a bizinesi .

Malinga ndi wailesi ya Vatican, Episkopi wa dayosizi ya Namibe ya mpingowu ambuyeDionisious Hisilinapo wati  anthu akumidzi m`dzikolo akulandidwa malo omwe anasiyilidwa ndi makolo zomwe zikudzetsa mavuto akululu pakati pawo.

Malo omwe anthuwa akulandidwa ati kwambiri akuti ndi omwe amagwilitsa ntchito  podyetsera ziweto zawo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>