Papa Alandira a Kazembe a Mmayiko Ena
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco analandira akazembe a mmaiko a Estonia, Malawi, Namibia, Seychelles, Thailand ndi Zambia komwe akazembewa amapereka makalata awo...
View ArticleMwambo Wodzoza Udikoni
Mwambo wodzoza asemino 13 kukhala adikoni wachitika Loweruka pa 21 May 2016 Ku Zomba Cathedral mu dayosizi ya Zomba ndipo Ambuye Desmond Tambala episkopi wa Dayosiziyi ndi amene azodza adikoniwa ....
View ArticleAkhristu Eni Azipereke Polimbikitsa Mpingo Wozidalira
Atsogoleri atsopano a bungwe loyimira akhristu eni mu mpingo wakatolika awapempha kuti adzipeleke pa ntchito yolimbikitsa akhristu pa za mpingo wodzidalira. Mlangizi wa bungwe-li mu mpingo wa katolika...
View ArticleKatswiri Wazisuzo ‘Izeki’ Wamwalira
Mmodzi mwa akatswiri azisuzo mdziko muno John Nyanga yemwe amatchuka ndi dzina loti Izeki wamwalira lamulungu masana ku chipatala chachikulu cha Queen Elizabeth mu mzinda wa Blantyre. Mzake yemwe...
View ArticleMabungwe A Mipingo Athandize Pa Bilu Ya Migodi
Bungwe la Norwegian Church Aid m’dziko muno lapempha mabungwe omwe si a boma makamaka amene ali amipingo kuti athandize boma pa ndondomeko yowunikiranso bwino bilu ya migodi. Mkulu wa bungwe la...
View ArticleApempha Akhristu Athandize Seminale Ya St. Peters
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awapempha akuti adzipeleke pa ntchito yosamalira seminale yayikulu ya St. Peters yomwe ili mu Dayosizi ya Zomba. Mkulu woyendetsa ntchito za seminalyi bambo...
View ArticleMOAM Yakhumudwa Ndi Anthu Okwera Minibus
Bungwe la eni minibus m’dziko muno laMinibus Owners Association of Malawi (MOAM) lati ndilokhumudwa kuti anthu okwera ndi amene akuthandizira kuti ma minibus m’dziko muno azinyamula anthu mopyola...
View ArticleMpingo Udzudzula Boma Polanda Malo Kwa Anthu Akumidzi
Mpingo wa katolika m`dziko la Angolawa dzudzula m`chitidwe wa akuluakulu a boma omwe akumalanda malo anthu a kumidzi ndi ku ma kawapeleka kwa anthu a bizinesi . Malinga ndi wailesi ya Vatican, Episkopi...
View ArticleParish Ya St. Anna Ichita M’bindikiro
Parish ya mpingo wakatolika ya St. Anna ku Kapire mu dayosizi ya Mangochi yati imadziwa zakufunika kolimbikitsa moyo wauzimu pakati pa akhristu ake. Bambo mfumu a parishi-yi bambo Danasio Malajira...
View ArticleUTATU WOYERA NDI CHIPHUNZITSO CHA UMODZI
Amayi a mpingo wa katolika omwe amatumikira Mulungu kudzera m`maimbidwe awapempha kuti azikhala ogwirizana monga Utatu oyera wa Mulungu atate,Mulungu mwana ndi Mulungu mzimu oyera. Sister Agatha...
View ArticleANTHU OTHAWA KWAO ASIMBA LOKOMA
Dziko la Greece layamba kusamutsa anthu ena othawa kwawo omwe amakhala pa malo ena otchedwa idomeni ndikukawaika ku malo ena kufupi ndi malire a dziko la Macedonia. Malingana ndi malipoti a wailesi...
View ArticleAnthu Atatu Afa pa Chiwonetsero cha Zipani Zotsutsa Mdziko la Kenya
Anthu atatu afa kumvuma kwa dziko la Kenya potsatira ziwonetsero zosakondwa za zipani zotsutsa boma zofuna kuti bungwe loyendetsa chisankho mdzikolo lisinthe ena mwa malamulo ake. Malipoti a wailesi ya...
View ArticleAnthu Khumi Afa pa Ngozi ya Bus
Anthu khumi afa ndipo ena 62 avulala bus yomwe anakwera itachita ngozi mdera la Songo mdziko la Mozambique. Malinga ndi malipoti bus-yo yomwe ndi ya Kampani ya Nyamende nambala yake KMZ 56 ZN...
View ArticleBungwe la CFT Lakonza Ndondomeko Zokweza Malonda Mdziko Muno
Bungwe lowonetsetsa kuti pakukhala chilungamo pa nkhani za malonda komanso kuteteza anthu ogula m’dziko muno, la Competition and Fair Trading (CFT) lati lakonza ndondomeko za tsopano zomwe zithandize...
View ArticlePapa Wati Kuyera Sikuchita Kugulidwa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti ngati akufuna kudzakhala oyera, sakuyenera kuchita manyazi potsatira zomwe Mulungu amafuna. Papa amalankhula izi pa...
View ArticleAkhristu Akatolika Akonzekere Bwino Lamulungu La Pa 29 May 2016
Mpingo wakatolika m’dziko muno wapempha akhristu a mpingowu kuti akonzekere bwino tsiku la mulungu la pa 29May2016pomwe akhristu a mpingowu apemphedwa kuti adzathandize seminale ya StPeter’s yomwe ili...
View ArticlePapa Wati Ndi Udindo Wa Aliyense Kusamalira Ndi Kuteteza Ana
M'tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisko wati ndi udindo wa munthu aliyense kuwonenetsetsa kuti ana akulandira chisamaliro ndi chitetezo chabwino. Papa walankhula izi lachitatu...
View ArticleAsilikali Apulumutsa Ana 53 Omwe Anabedwa Ku Ethiopia
Asilikali m’dziko la Ethiopia ati akwananitsa kupulumutsa ana makumi asanu ndi atatu 53 omwe anabedwa ndi gulu lina la zigawenga m’dzikomo. Malingana ndi malipoti a wailesi ya BBC anawa akuti anagwidwa...
View ArticleUlendo wa Ku Uganda Wapsya
Bungwe la abwenzi a amalitiri aku Uganda lati zokonzekera za ulendo wokayendera malo oyera a Namugongo omwe amalitiri anaphedwera m’dziko la Uganda chaka chino zayenda bwino. Malinga ndi wapampando wa...
View ArticleBungwe la CCJP Lipempha Boma Lilipire Msanga Aphunzitsi ku Nsanje
Bungwe la chilungamo ndi mtendere mu dayosizi ya Chikwawa ya mpingo wakatolika yapempha boma kuti likonze msanga malipiro a aphunzitsi a m’boma la Nsanje omwe mpaka pano sanalandire malipiro awo a...
View Article