Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mariatona Kathithi Wayamba

$
0
0

Radio Maria Malawi yayamba masiku atatu a Mariatona wa kathithi ngati njira imodzi yofuna kupeza ndalama zokwana 30 million kwacha yothandizira wailesiyi kuti imange studio yatsopano ku Limbe Cathedral mu arkidayosizi ya Blantyre.

Malinga ndi m’modzi mwa akuluakulu a wailesiyi a Emmanuel Kaliati, kuyambira lachisanu mpaka lamulungu wailesiyi ikhala ikuwulutsa ma pologalamu okhudza mariatona okhaokha momwe anthu azilonjeza ndalama yomwe apereke ku wailesiyi mu mariatona-yu.

AIwo ati ngakhale mariatona wa kathithi atatsekedwe lamulungu likudzali, mariatonayu akhale akupitilirabe ndipo adzatha pa 10 December chaka chino.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko