Apolisi 6 Aphedwa mu Mzinda wa Kirkuk Mdziko la Iraq
Apolisi asanu ndi m’modzi 6 komanso anthu ena 16 afa pa chiwembu chomwe gulu la za uchifwamba la Islamic state lachita pa nyumba za boma mu mzinda wa Kirkuk mdziko la Iraq. Malipoti a wailesi ya BBC...
View ArticleMariatona Kathithi Wayamba
Radio Maria Malawi yayamba masiku atatu a Mariatona wa kathithi ngati njira imodzi yofuna kupeza ndalama zokwana 30 million kwacha yothandizira wailesiyi kuti imange studio yatsopano ku Limbe Cathedral...
View ArticleAlipira 1.8 Million Kaamba Kopha Anthu Poyendetsa Galimoto Mosasamala
Bwalo la milandu m’boma la Mangochi lalamula mkulu wina wa zaka 25 zakubadwa kuti alipire ndalama zokwana 1 million 8 hundred 50 thousand kwacha kapena kukakhala ku ndende ndi kukagwira ntchito ya...
View ArticleNgozi za pa Nsewu Zachepa ndi 39 Percent
Ngozi za pansewu m’dziko muno akuti zachepa ndi 39 percent m’miyezi isanu ndi inayi 9 yapitayi poyerekeza ndi nthawi ngati yomweyi chaka chatha. Wofalitsa nkhani za apolisi mdziko muno a James...
View ArticleAbayana ndi Mpeni Pachibale
Apolisi m’boma la Ntchisi akusunga mchitokosi mnyamata wina wa zaka 15 zakubadwa kaamba komuganizira kuti wavulaza mchimwene wake pomubaya pa mtima ndi mpeni. Wapolisi wofalitsa nkhani m’bomalo Sergent...
View ArticleAkayidi 170 Athawa ku Ndende Mdziko la Haiti
Akaidi oposa 1 hundred 70 athawa mu ndende ina kumpoto kwa dziko la Haiti. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, akaidi omwe athawawo ati aba mfuti zisanu ndi kupha mulonda m’modzi wa pa malowa...
View ArticleSACCO Yapereka Zipangizo ku Chipatala cha Dedza
Bungwe la aphunzitsi losunga ndi kubwereketsa ndalama la SACCO m’chigawo cha pakati lapereka zipangizo zogwiritsa ntchito pa chipatala cha boma la Dedza. Malinga ndi wamkulu wa bungweli a Henry...
View ArticleRadio Maria Malawi itsekera masiku atatu a Mariatona Kathithi
Radio Maria Malawi yatsekera masiku atatu a Mariatona wa kathithi. Malinga ndi m'modzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za wailesiyi a Emmanuel Kaliati, mariatona kathithiyu atsekeleredwa ndi mwambo...
View ArticleAkhristu a Parish ya Thondwe Athandiza Chipatala cha Zomba
Akhristu a mpingo wa katolika mu parishi ya St. Anthony Thondwe apereka thandizo la katundu wosiyanasiyana kwa odwala a pa chipatala chachikulu cha boma la Zomba. Malinga ndi bambo mfumu a parishiyi...
View ArticleBoma Lipempha Anamwino Agwire Ntchito Modzipereka
Boma lapempha anamwino mdziko muno kuti azigwira ntchito yawo molimbika, mokhulupilika komanso modzipereka. Nduna ya zaumoyo Dr. Peter Kumpalume apereka pempholi pa mwambo wopereka ma diploma ndi ma...
View ArticleAkhristu Azipemphera Kolona pa Goroto
Akristu a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti azikonda kupemphera kolona pogwiritsa ntchito goloto la Amai Maria. Wapampando wa bungwe la Legio Ya Mariamu parishi ya Likuni mu arkidayosizi...
View ArticleOfesi Yowona Za Chipembedzo Itsekedwa Mdziko la Canada
Kutseka kwa ofesi yowona za ufulu wa chipembedzo mdziko la Canada ati kuchititsa kuti anthu aziphwanyiridwa ufulu wa azipembedzo komanso azikhala ndi mantha. Mmodzi mwa akuluakulu omenyera ufulu wa...
View ArticleFather Cosmass Maleka Dies
The Catholic Secretariat of the Episcopal Conference of Malawi regrets to announce the death of Fr. Cosmas Maleka of the Diocese of Dedza. Fr. Maleka has passed away today, November 1, 2016 after being...
View ArticleBambo Cosmass Maleka Atisiya
A kulikulu la mpingo wakatolika m’dziko muno ku Episcopal Comference of Malawi(ECM) alengeza za imfa ya bambo Cosmass Maleka omwe amatumikira mpingo-wu mu dayosizi ya Dedza. Bambo-wa amwalira galimoto...
View ArticleAmbuye Chamgwera Ayamikira Parishi ya Cobbe Barracks
Akhristu a m’parishi ya Holy Family Cobbe Barracks mu dayosizi ya Zomba awayamikira kaamba kodzipereka pomanga tchalitchi latsopano lalikulu komanso lokongola. Episkopi wopuma wa dayosiziyi Ambuye...
View ArticlePapa Apemphera Limodzi ndi Mpingo wa Lutheran Mdziko la Sweden
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisco anachita mapemphero limodzi ndi akhristu ampingo wa Lutheran mdziko la Sweden. Malinga ndi malipoti a wayilesi ya Vatican, mapempherowa...
View ArticleKuyenderana Pakati pa a Payomo, Goretti M’maparish Kumapititsa Chipembezo...
Kuyenderana pakati pa achinyamata a PAYOMO komanso Maria Goretti akuti kungathandize kupititsa patsogolo chipembezo ndi kuzamitsa moyo wa chikhristu pakati ana mu mpingo wakatolika. Mkulu woyang’anira...
View ArticleCardinal Filoni arrives in the country for Karonga Cathedral Consecration
At exactly 2:15 pm, His Eminence Fernando Cardinal Filoni arrived at Kamuzu International Airport (KIA) ahead of the consecration of St Joseph the Worker Cathedral of the Catholic Church in Karonga...
View ArticleCardinal Filon Wafika Mdziko Muno
Cardinal Fernando Filoni wafika m’dziko muno lero kuti adzakhale nawo pa mwambo wokhazikitsa Cathedral ya dayosizi ya Karonga loweruka likudzali, m’malo mwa mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko...
View ArticlePapa Wayamikira Atsogoleri a Zipembezo Zosiyanasiyana
M'tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira atsogoleri a zipembedzo zosiyanasiyana kaamba kofika ku msonkhano umene iye anayitanitsa ku likulu la mpingowu ku Vatican. Papa...
View Article