Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

ZOKONZEKERA MSONKHANO WA AMECEA ZIKUYENDA BWINO

$
0
0

Committee yoyendetsa zokonzekera za msonkhano wa ma Episcopi a chigawo cha ku m'mawa ndi pakati muno mu Africa la AMECEA mu m'zinda wa Lilongwe yati ndiyokhutila ndi zokonzekera za msokhanowu.

Wapampando wa committee yowona zotolereza chuma mayi Dr. Mary Shawa ndi yemwe wafotokozera izi ofesi ya zofalitsa nkhani ku likulu la mpingo wa katolika ku Lilongwe. Mayi Shaba amafotokoza izi pokhutila ndi anthu akufuna kwa bwino omwe anabwera ku nkhumalilo komanso chiphwando cha mayimbidwe chomwe anakonza lachisanu sabata yatha mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi mayi Dr. Shaba,committee yawo ikuyembekezeka kupeza ndalama pafupifupi 700 thousand  US Dollas  kuti msonkhanowu udzayende bwino. Msonkhanowu udzachitika kuyambira pa 16 mpaka pa 26 July chaka cha m'mawa.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>