CHURCHES OF CHRIST IKUDZIPEREKA PA NTCHITO ZA CHIFUNDO
Mpingo wa CHURCHES OF CHRIST m’boma la MANGOCHI wati ukudzipeleka kwambiri pogwira ntchito za chifundo pambalinso pogwira ntchito zofalitsa uthenga wa chipulumutso, M`busa Denson Mulaleya wa mpingowu...
View ArticleMNYAMATA WA ZAKA 17 APHA MCHEMWALI WAKE KU MANGOCHI
Apolisi m’boma la Mangochi akusunga mchitolokosi mnyamata wina wa zaka 17 kamba komuganizira kuti anamenya ndikupha mchemwali wake. MneneRi wa apolisi m`bomalo Inspector Rodrick Maida, watsimikizira...
View ArticleANTHU ASAFE NDI NJALA - VOICE OF THYOLO
Bungwe la Voice of Thyolo m`boma la Thyolo, ladzudzula boma, kaamba kolekelera kuti anthu omwe anathawa kudera la Mfumu yayikulu Ngonamo kwa Mfumu yayikulu Thomasi m`bomalo, adzimwalira ndi njala...
View ArticleSITIKUTEKESEKA NDIKUCHOKA KWA APHUNGU - DPP
Chipani cha Democratic Progessive {DPP} chati sichikutekeseka ndikuchoka kwa aphungu ena m'chipanichi kukalowa chipani cholamula cha PP. Mneneri wachipanichi a Nicholas Dausi,anena izi pomwe phungu...
View ArticleKodi Chokhalitsa Nchiyani
New Ulaliki titled Kodi Chokhalitsa Nchiyani by Father Clement Mmana
View ArticleChiminingo Cha Mulungu Chimaposa Cha Munthu Wina aliyense
Ulaliki titled Chiminingo Cha Mulungu Chimaposa Cha Munthu Wina Aliyense by Mai Senia Kaunda
View ArticleMaiko Onse Tikondane
Song Maiko Onse Tikondane by St Cecilia Sigerege Of Blantyre Diocese
View ArticleEPISIKOPI WA DAYOSIZI YA BERGAMO AYENDERA RADIO MARIA MALAWI
Episikopi wa diyosizi ya Mangochi ya Mpingo wa Katolika Ambuye Allesandro Pagani ayamikira ubale umene ulipo pakati pa diyosiziyi ndi diyosizi ya Bergamo m’dziko la Itary. Ambuye Pagani alakhula izi...
View ArticleZIPANI ZA NDALE ZIKHALE NDI MFUNDO ZENIZENI”-DR. CHINSINGA
Katswiri pankhani zandale yemwenso ndi mphunzitsi kusukulu ya Chancellor College Dr. Blessings Chinsinga wati nthawi yakwana yoti atsogoleri andale komanso zipani ziyambe kukonza ndi kufotokozera a...
View ArticlePAPA FRANCIS WATSEKULIRA CHAKA CHA ACHINYAMATA
Mwambo wa nsembe ya misa yotsekulira chaka cha achinyamata wachitika ku copacabana mu arch diocese ya Rio ya mpingo wa katolika m’dziko la Brazil. Mtsogoleri wa Mpingo wa katolika pa dziko lonse...
View ArticleANTHU OKWIYA AVULAZA ABALE A MFUMU KU NTCHISI
Anthu ena ozungulira dera la mfumu Chikho mboma la Ntchisi avulaza abale a mfumu ya deralo komanso kuwononga katundu wa ndalama zoposa 117 thousand pokwiya ndi ulamuliro wa mfumuyo. Mneneli wa apolisi...
View ArticleAWAPEMPHA KUTI AKALEMBETSE MWAUNYINJI MU KAUNDULA WA CHISANKHO
Anthu a m’dera la Mfumu Yaikulu Amidu m’boma la Balaka awapempha kuti akalembetse mwaunyinji mu kaundula wa chisankho kuti akhale ndi mwayi wodzaponya voti pa chisankho cha chaka cha mawa. Mmodzi...
View Article“MUSALOWETSE CHINYENGO PA NTCHITO ZA CHITUKUKO”-SIMPLEX CHITHYOLA
Mabungwe omwe siaboma amene akugwira ntchito zao m’boma la Balaka, awapempha kuti azigwira ntchito zawo mopanda chinyengo komanso mofuna kutukula miyoyo ya anthu mbomalo. Wapampando watsopano wa komiti...
View ArticleNASAF IPEREKA NGONGOLE YA MATRACTOR NGATI NJIRA IMODZI YOPITITSIRA PATSOGOLO...
Mtsogoleri wa chipani cha National Salvation Front NASAF a JAMES NYONDO watsindika kuti ntchito yomwe walonjeza yopeleka ngongole ya ma TRACTOR kwa alimi a m’dziko muno siyankhambakamwa chabe ndipo...
View ArticleZOKONZEKERA MSONKHANO WA AMECEA ZIKUYENDA BWINO
Committee yoyendetsa zokonzekera za msonkhano wa ma Episcopi a chigawo cha ku m'mawa ndi pakati muno mu Africa la AMECEA mu m'zinda wa Lilongwe yati ndiyokhutila ndi zokonzekera za msokhanowu....
View Article